Chapitan 9

1 Ndipo mafumu yonse yanakhala kusogolo kwa Yolodani muziko ya mapili, na malo ya pansi ya munyanja kufupi na Lebanoni - mu Hittites, Amoni, Akanani, Aperizzites, Hivites, na ajebusites - 2 Zonse zina lumikizanz pansi pa lamulo imozi, kuchaya nkhondo na Yoswa na Israyeli. 3 Pamene bonkhala mu Gbeoni banamva vamene Yoswa anacita kuyeliko na ku Ai, 4 Banapanga mapiani mocenjeia, Banayenda monga amithenga Banatenga masaka yong'ambika nakuyafakaa pa mabulu banatenganso vikumba va vinyu wakudala vong'ambika, ndipo vinakonzewa. 5 Bavala nsapato zakale na zongambika kumapazi yao, nakuvala vakale, vovala vong'ambika, mikate yonse muumalo yosungilamo inali yoyuma. 6 Ndipo banayenda kuli Yoswa mucipono ca Giligala nakukamba naye naba muna ba mu Israyeli,'' tacokela kuziko yakutali, Apa manje panga cipangano naise.'' 7 Bamuna bamo Israyeli banakamba kuli ba Hivites, '' kapena munkhala pafupi naise. Tingapange bwanji cipangano naimwe?'' 8 Banamba kuli Yoswa kuti,'' Ise ndise batumiki bano.'' Yoswa anakamba na beve, '' Ndiwe ndini? munacokele kuti?'' 9 banakamba kuli iye,'' Batumitiki bako babwela kuno kucokela kumalo yakutali, cifukwa ca zina ya Yehova mulungu wanu. Tamvela pali yeve na pali vonse anacita mu Eigipito - 10 navonse anacita kuli mafumu yabili yako Amoni kumbali ina ya Yolodani - kuli sihon mfumu ya Heshbon, na ku og mfumu ya Bashan amene enze pa Ashtaota. 11 Bakulu banthu na bonse bonkhala muziko banakamba naife,' nyamulani vokudya muulendo wanu. Yenda kukumana nabeve na kukamba nabo,'' ndife batumiki banu pangana ni nafe,'' 12 Uyu ndife mkate wanu, vnali ukuli wakupsa pamene tina utenga kucosa manyumba yathu pasiku tinacoka kubwela kuli imwe koma manje, ona, niyo yuma na kuzizila. 13 Ivi vikumba va vinyu vakale vinali va nyowani pamene tinavi zuza manje ona, manje vinang'ambika vovala vathu na nsapato zathu zasilila ku olendo utali 14 Pamenepo ba Israyeli banatenga vokudya vina, koma sanafunse Yehova kubabuza vocita. 15 Yoswa anapanga mutendele na beve na kupanga cipangano nabeve, kubasiya na moyo. Basogoleli babanthu nabeve banalumbilila kuli beve. 16 Masiku yatatu bana ba Israyeli atapanga cipangano na beve, banamvela kuti banali kukhala nabo pafupi. 17 Ndipo bana ba Israyeli banayambapo nakufika kumizinda yao pasiku yacitatu. mizinda yao yanali Gibeoni, Kephirah, Beeroth, na Kiriath Jearim. 18 Bana ba Israyeli sanabamenye cifukwa basogoleli bao banalumbulila pali beve pamenso ya Yehova, mulungu wa Israyeli, Ba Israyeli bonse banali kudandavla pali asogoleli bao. 19 koma basogoleli bonse banakamba kuli banthu bonse,'' tina ba lumbililako kwa Yehova, mulungu wa Israyeli, manje sitinga bacite. 20 Izi ndiye tizacita kuli beve: kupewa ukali wamene ungabwele pali ise cifukwa ca lumbilo yamene tinalapa kuli beve.'' 21 Basogoleli banakamba kuli banthu bao,'' nkhala na moyo.'' ndipo ba Gibeonites banakhala wojuba maplanga na botapa mazi ya bana ba Israyeli, monga mwamee ba sogoleli anakambila pali beve. 22 Yoswa anabaitana na kukamba kuti, '' cifukwa nicani ananinama pamene unakamba, tili kutali naimwe,' pamene ukhala pakati kaise? 23 Manje, cifukwa caici, ndiwe otembeleleka nabena baimwe muzayamba kukhala akapolo, naja wodula maplanga na botapa manzi ya nyuma ya mulungu.'' 24 Banayankha Yoswa na kukamba kuti,'' cifukwa cinauziwa kuli batumiki kuti Yehova mulungu analamulila mtumiki wake Mose kukupasani malo yonse, nakubononga bonse bokhala mumalo pamenso yanu - ndipo ticitila miyoyo yathu mantha cifukwa ca ino. Cifukwa cake tinacita cinthu ici cinthu. 25 Manje, ona, utigwila mu mphamvu yako. ciliconse coboneka cabwino na colungama kucitila ife, cita.'' 26 Potelo Yoswa anabacitila ici: Anabacosamo muulamulilo wa bana ba Israyeli, kuti Israeli basaba paye. 27 Siku yame Yoswa anakumana nabo juba maplanga ma Gibeonites na botapa manzi mu muzi, na paguwa ya Yehova, paka lelo, mumalo yamene Yehova anasankha.