Chapita 10

1 Manje pamene Adoni - Zedeki, mfumu yaku Yelusalemu, inamva kuti Yoswa anatenga Ai nakuionongelatu (monga mwamene banacitilaku Yeliko na mfumu yake), anamvelanso mwamene bantu ba ku Gebeoni banapangila mtendele na Israyeli nakunkhala pakati kao. 2 Bana ba Israyeli banayopa maningi cifukwa Gibeoni inali muzinda ukulu, monga umozi wamuzinda wa mfumu. Vnali ukulu kucila Ai, nabamvna bonse banali bankhondo bamphamvu. 3 Cifukwa cake Adoni - Zedeki, mfumu yaku Yelusalemu, anatuma wamtenga ku Honami, mfumu yaku Hebroni, ku Piram, mfumu yako Jaruta, ku Jaaphia, mfumu yako Lachish, na ku Debir, mfumu yaku Egloni: 4 ''Bwela kulibe nakunithandiza ine. Tiyeni timenye Gibeoni cifukwa bapanga mtendele na Yoswa na bana ba Israyeli. 5 Mafumu yali (5) faivi ya Amoni, mfumu yaku Yelusalemu, mfumu yaku Hebroni, mfumu yaku Jarmuth, mfumu yaku Lachish, na mfumu yaku Egloni banabwela, beve nabonse bankhondo bao. Banakhala malo yao kunyamukila Gibeon, na kumumenya. 6 Bantu baku Gibeoni banatuma uthhenga ku Yoswa naba nkhondo baku Giligala, Banakamba kuti, ''yendesani! Osacosako manje yanu kuli mtumiki wanu bweleni ku ife mwamsanga na kuti pulumusa. Tithandizeni ise, popeza mamfumu yonse ya Amori bamene bakhala ma piri ya muziko bakumana pamozi kuti menya.'' 7 Yoswa anayenda ku giligala, iye nabonse bamuna ba nkhondo na bonse bomenya nkhondo. 8 Yehova anakamba kuli Yoswa,'' osabayopa. Nabapasa mumanja yanu kulibe umozi pali beve azakulesa kumenya kwanu.'' 9 Yoswa anabwela pali beve mwazizizi, batayenda usiku bonse kucoka ku Giligala. 10 Yehova anasokonoza mudani pamenso ya Israyeli, Israyeli anabapaya na kukanthidwa kokulu pa Gibeoni na ku bapepeka panjila yoyenda ku Beth Horon, na kubapaya panjila yaku Azekah naku Makkedah. 11 Pamene banali kuthaba Israyeli, pansi pa phili kucoka ku Beth Horon, Yehova anaponya miyala yakulu pansi kucoka kumwamba pali beve njira yonse paku ku Azekah, nipo anamwalila. Banali bambili banafa namatalala kucila banafa namapanga ya bamuna ba Israyeli. 12 Pamenepo Yoswa anakamba na Yehova pasiku yamene Yehova anapasa bamuna ba Israyeli kupambana pali ba Amoni. Izi ndiye zamene Yoswa anakamba, ''Zuba, imilila, pa Gibeoni, na mwezi, mu cigwa ca Aijalon.'' 13 Zuba ina imilila, na mwezi unaleka kuyenda paka ziko inabwezela cilango pali badani bao. Kodi izi sizinalembewe mu buku ya Jashar? Zuba inakhala mukati mwa mitambo; sinangena siku yonse. 14 Sukunankhalepe siku yatele kudala kapene kusogolo, pamene Yehova anamvelela mav ya banthu. Popeza Yehova anali kumenyelaka Israyeli nkhondo. 15 Yoswa na Israyeli pamozi banabwelela kucigono ku Giligala. 16 Manje mafumu yali faivi yanathaba na kuzibisa mumakavu pa makkedah. 17 Zinabuziwa kuli Yoswa,'' bapezeka! - mafumu yali faivi (5) yobisamu muma kavu ya makkedah!'' 18 Yoswa anakamba kuti, kukhvnizilani miyala ikulu pakamba ka kavu nakvikapo basilikali kuti basungepo. 19 Osankhala imwe, pepekani badani banu na kubamenya ba mumbuyo. Osabavomekeza kungena mu mizinda yao, cifukwa Yehova mulungu wanu abapasa mu manja mwanu.'' 20 Yoswa na bana ba Israyeli banasiliza kuba kantha nakukantha kukulu, paka banali pafupi kusililatu; Bang'ono cabe opulumuka banafika mizinda ya malinga. 21 Pamene gulu yonse yankhondo inabwelela mwamtendele kuli Yoswa ku cigono pa makkedah, kulibe wamene anayesa kukamba mav yamozi pali bana ba Israyeli. 22 Pamene Yoswa anakamba kuti,'' segulani pakamwe ka kavu nakucosela mukavu mfumu zili faivi (5).'' 23 Banacita mwamene anakambila. Banamuletela mafumu yali faivi (5) kucoka mu kavu - mfumu ya Yelusalemu, mfumu yaku Hebron, na mfumu yaku Jarmuth, na mfumu yaku Lachish, na mfumu yaku Egloni. 24 Ataleta mfumu kuli Yoswa, anaitana munthu alibonse wanu Israyeli. Anakamba kuli bakulu ba asilikali bamene banayenda kunkhondo nayeve,'' fakani mapazi yanu pamikosi yabo.'' Pamenepo banabwela na kufaka mapazi yabo pamikosi yabo. 25 Banakamba kuli beve,'' osayopa na kuda nkhawa. Khalani okosa na mphamvu. Izi ndiye zamene Yehova azacita kuli badani bonse bamene muzamenyana nabo.'' 26 Pamenepo Yoswa anamenya na kupaya mafumu. Anabapacika pamitengo zili faivi (5) anapacikiwa pamitengo paka mazulo. 27 Pamene zuba inangena, Yoswa anapasa malamulo, nakubaselusa mumitengo naku bataila mu kavu kwamene benze banabisama. Banaika miyala yakulu pakamwaka kavu, miyala yaja yakalipo pakana lelo. 28 Munjila iyi, Yoswa anatenga makkedah pasiku ija nakupaya alibonse muja napanga, kufakilako namafumu yabo. Anabonongelatu alibonse bokhalamo. sanasiyeko apulumuka alibonse. Acita kuli mfumu yaku makkedah mwamene anacitila kuli yaku Yeliko. 29 Yoshuwa na yonse Isirayeli inapita kuchoka ku Makedaya kuyenda ku Libina. Anayamba nkondo na Libina. 30 Yehova anaipasa mumanja ya Isirayeli-pamozi na mfumu yao. Yoshuwa anaononga na mupeni nakupaya muntu ali onse anali mo. Sanasiyemo muntu ali onse wamoyo. Anachita kuli mfumu yabo monga mwamene anachitila kuli mfumu ya Yeliko. 31 Ndipo Yoswa na Israyeli bonse anapitilila kucoka ku Libnah kuyenda ku Lachish. Anamanga misasa naku menya nkhondo pamenepo. 32 Yehova anapasa Lachishi mu manja ya Israyeli, Yoswa anaitenga pasiku yacibili na kuikantha napanga ya kutwa na munthu alibonse okhalamo, mwamene anacitila ku Libnah. 33 Pamenepo Horam, Mfumu yaku Gezer, anabwela kuthandiza Lachish. Yoswa anamenya iye paka kunalibe loko umozi opulumuka anasalako. 34 Ndipo Yoswa na Israyeli bonse bana pitila kucoka ku Lachish kuyenda ku Egloni. Banamanga misakasa nakumenya ziko ija, 35 nakuitenga siku yamene ija. Banaikantha na panga yakutwa na kubonongelatu alibonse okhala mo, mwamene Yoswa anacitila kuli Lachishi. 36 Ndipo Yoswa na Israyeli bonse banapitila kucoka ku Eglon kuyenda ku Hebroni. Banamenya nkhondo nayeve. 37 Banaitenga, nakvikantha napanga uakutwa, pamozi na mafumu yabo na mizi zao, nabanthu bonse bokhalamo. sibanasiyeko opulumuka, monga mwamene banacitila ku Egloni, banabonongelatu nabonse bokhalamo. 38 Pamenepo Yoswa anabwelela, naba nkhondo bonse ba Israyeli nayeve, nakupitila ku Debir na kumenya nkhondo nabeve. 39 Banaitenga, mfumu yabo na mizi yonse yapafupi. Banabakantha napanga yakutwa nakubonongelatu munthu alibonse bokhalamo. sibanasiyeko opulumuka. Banacita kuli Debir mwamene banacitila kuli Libnah na mfumu yabo na kuli Hebron. 40 Yoswa anakantha ziko yonse, ya kuma pili, ya kumwela, ya kumadimba na kuzigwa. pa mafumu yonse sanasiyeko alibonse opulumuka. Anabonongelatu ciliconse camoyo, monga mwamene Yehova, mulungu wa Israyeli, analamulila. 41 Yoswa anabakantha kocokela ku kadesh Barnea mpaka ku Gaza, na maiko yonse ya ku Gosheni mpaka ku Gibeon. 42 Yoswa anatenga mafumu yonse namalo yabo panthawi imozi cifukwa Yehova, mulungu wa Israyeli, anamenyela Israyeli. 43 Pamenepo Yoswa, na Israyeli bonse, banabwelela kucigono ku Giligala.