Chapita 16

1 Gabo ya malo ya mtundu wa Yosefe yanakulila kucoka ku Yolodani pa Yeliko, kumawa kwa cisime ca Yeliko, mucipululu, kuyenda kumwamba kucoka ku Yeliko kupitila muphili yaziko ya ku Beteli. 2 Pamenepo inacoka ku Beteli kuyenda ku tuzi na kupiitila njila yaku Adaroth, malo ya Arkites. 3 Ndipo inaselikila kumazulo kwa malo yaba Japhletites, kutali monga manga malo ya pansi Beth Horoni, na ku Gezer; inasilila pa nyanja. 4 Inali munjila kyi kuti mitundu ya Yosefe, manase na Eflemu yanalandila coloba cabo. 5 Malo ya mutundu wa Eflemu, banja pabanja; malila yacoloba cabo kumawa yanacokela ku Ataroth Addar kufika kumwamba kwa Beth horon, 6 nakucoka kuja inapitiliza kuyenda kunyanja. Kucoka ku mikmethath ku mpoto inakonekela kumawa kufupi na Taanath shiloh nakuipitilila kumawa kwa Janoah. 7 Pamenepo inayenda pansi kucoka ku Janoah kuyenda ku Ataroth na ku Naarah, na kufika pa Yeliko, kusilizila pa Yolodani. 8 Kuyambila ku Tappuah malile yana yenda kumazulo kwa musinje wa kanah naku silizila pa nyanja. Ndiye cinali coloba ca Eflemu, banja pa banja, 9 Pamozi namizinda yamene yanasankhiwa yamitundu ya Eflamu pamozi na coloba ca mutundu wa manase mizinda yonse kufukilako mizi zao. 10 Sabanacose Akanani bamene banakhala mu Gezer kuti Akanani akhala pakati ka Eflamu kufika lelo, koma banthu bana pangiwa kupapa mokaka miziwa.