Mutu 44

1 Yosefe analamulila wanchito wa munyumba yake, ku kamba kuti, "Zulisa vakudya m'masaka ya bamjuna, kulingana na vamene bangakwanise kunyamula, ndipo ayike ndalama zake aliyense posengula saka yake. 2 Uyike kapu yanga, ija ya siliva, pakamwa posegulila saka ya ija mungono paonse, na ndamala yake ya cakudya."Wanchito wa Yosefe anachita monga mwamene ana mu uzila. 3 Kuseni seni, ndipo bamuna aba banabauza bayende banatenga na ba buru bao. 4 Pamene banacoka m'mzinda koma Sbana fike patali maningi. Yosefe anakamba ku wa nchito wake, "Nyamuka, konka ba muna, ndipo ukubapitilila, ubauze kuti, 'Nchifukwa chani mwa bwezela choipa pa cha bwino? 5 Kodi iyi si kapu yamene abwana banga bama mmwela, na kapu yamene ba ma ombezelako? Ichi chintu chamene mwa chita, mwa chita choipa." 6 Wanchito anavapitilila na ku bauza mau Mau. 7 Bamu uza, "Nichani ba bwana banga bakamba mau monga aya? Ichi chintu chisankale na banchito ku chita cha mutundu uyu. 8 Ona ndalama tinapeaza mosegulila masaka yatu, "yamene tinabweesa futi kuli kuchokeku Canani. Manke tingabe bwanji mu nyumba ya ba bwana bako siliva na golide? 9 Ngati aliwonse pali ba nchito bako apezeka nayo, mutekeni amwalile, na ife tizankala ba kapolo ba mfumu wanga." 10 Wanchito anakamba, Apa manje lekani chinkale monga mau yanu. Wamene azapezeka na kapu azankala kapolo wanga, koma imwe benangu m'mzakala mube mulandu." 11 Kuchoka apo munthu onse anayendesa nakubwelesa nakusitizila saka yake pansi, ndipo aliyense anasegula saka yake. 12 Wanchito ana sakila. Anayambila mukulu pali onse nakusilizila na mung'ono pa bonse, ndipo kapu inapezeka musaka ya Benjamini. 13 Apo bana ng'amba vovala vao. Munthu aliyense anaika katundu yake pali buru nakubwelela ku muzinda. 14 Yudah na abale nawo, "Nichani chamene mwachita ici? Simuziba kuti munthu monga ine nimachita zo-ombeza?" 15 Yosefe anakamba, "Tingakambe chani kwa bwana wanga? Tizakamba chani? Kodi tizazilungamitse bwanji? Mulungu aipeza chimo ya mbadwa mubanchito banu. Onani, ndife bakapolo ba bwana wanga, ise namwane kapu yapezeka mumanja mwake." 16 Yudah anakamba, "Tingakambe chani kwa bwana wanga? Tizakamba chani? Kodi tingazilungamitse bwanji? Muungu aipeza chimo ya mbadwa mubanchito banu. Ona, ndife bakapolo ba bwana wanga, Ise nawamene kapu yopezeka mumanja mwake. 17 Yosefe anakamba, "Chinkale patali naine cha mutundu uyu kuti ninga chichite, Munthu wamene enze apezeka na kape m'kwanja mwake, uyu munthu anzankala kapolo wanga, koma kwa imwe benangu mutende mwa mtendele kwa atate anu." 18 Kuchoka apo Yudah ababwela pafupi naye nakukamba, "'Mfumu yanga, anapapata lekani wanchito wanu akambeko ku munthu yanu, ndipo mu saleke ukali wanu kuti uyonekele pali kapolo wanu. Chifukwa imwe ni chimodzi modzi na Falao. 19 Bwana wanga inafunsa banchito bake, kakamba," uli na atate alo m'bale. 20 Tinakamba kwa mfumu, "Tilinayo atate, ba chikulile na mwana wamu ukote wayo muny'ono. Koma mbale wake anafa, ndipo eve aka ndiye anasalapo ya ba mayi bake, na batate bake bomukonda. 21 Ndipo munakamba kuli ba chinto banu,, mu bweleseni kiuli ine ni muone! 22 Kuchoka apo tinakamba kuli ba bwana banga, 'Munyamata sangasiye ba tate bake. Ngati abasiya batate bake bazamwalila. 23 Ndipo munakamba kuli banchito banu, koma chabe mu bwele na m'bela wanu wamung'ono simuzakaona pa menso panga futi. 24 Ndipo chanabwela kuti pamene tinaenda kuli banchito banu atate, tinoba ma ya abwana banga. 25 Atate batu banakamba yendani futi mukatigulile vakudia. 26 Ndipo tinakamba, "Sitinga yendeko khoma ngati,mubale wathu wamung'ono alina ife, Tiza endo, chifukwa chakuti sitizakwanisa kuona pamenso pa uja munthu. Koma chabe nufana wathu ankale naife.' 27 Akapolo wanu atate anga analamba kwa ife kuti'Mu ziba mukazi wanga anabala kuli ine bana ba muna babili. 28 Umodzi ananichoka ine ndipo ninakamba kuti, "Zoona anamujuba juba mu ziduswa duswa, 'kuchika apo sinina muonepo futi. 29 Apa manje mukatenga uyu kuli ine, na choipa chikumu bwelela, muzabwesa pansi imvi zanga na chikwinyilito ku manda. 30 Apa, manaje, nikafika ku wanchito wanu atate, tilibe mung'ono wathu, chifukwa moyo wake wamangila pali muyo wa munyamata uyu. 31 Chizachitika akaona kuti tilibe munyamata ife azamwalila. Ba kapolo banu bazabwelasa imvi za kapolo wamu atate mu chisoni paka kumanda. 32 Chifukwa kapolo wanu ine ninakala chisimikizo ca munyamata kuli batate nokamba kuti, ngati sinza bwela nayeve, kuli imwe, apo nizankala wa milandi kwa atate banga tawi zonse. 33 Kufika apa manje, napapata lekeni wa nchito wanu ankele mumalo mwa munyamata monga kapolo wa abwana banga,, nakuleka munyamata ayende nabale bako. 34 Ningabwelele bwanji kuli atate ngati munyamata sazankala naise? Niyopa kuyenda kuona voipa vinga bwele pali atate banga.