Mutu 43

1 Njala inapitila mu malo. 2 zinacitika pamene bana diya chakudya zamene bana bwelesa ku Igipito, ba tate babo bana kamba ku libeve, "Endani futi, tigulani vakudya." 3 Yudu ana bauza eo. " Munthu monenesa anaticejeza ife. 'Simuza ona nkhope yanga kufikila mubale wanu ngati ali naimwe.' 4 Ndati muza tituma namubale wathu, tiza enda pasi ndi ku gulalila imwe vakudia. 5 Ngati simumutuma eve, citi zaenda pansi, daba uyu munthu anakamba kwaise, simuza ona nkhope yanga pokapo mubale wanu ngatiali naimwe.'" 6 Israeli anakamba, " Chifukwa chani mwani chitila choipa pa kuniuza nyu munthu kuti mulina mubale wanu wina?" 7 Bana kamba, " Uyu munthu anati fusa mopitilila zaise ndi banja lathu, ana kamba,' batate banu balimoyo? Kodi muli na mubale wanu wina?' Tina mu yankha eve kulingana ndi mafuso yake. Sembe tina ziba bwanji zamene aza kamba, 'muletani mubale wanu pasi?'" 8 Yuda anakamba kwa Israeli, tate wake. " Mutumeni mwana na ife, tiza yamuka ndi ku yenda kuti ti nkhale moyo ndi kuti ti safe, bose ife, naimwe, ndi oso bana bathu. 9 Niza khala chosimikizilako kwa eve. Muza Muzanipasa muladu ine. Ngati siniza bwaza kwainu kumuonsa pamaso panu, ndipo lekani niyamule dadaulo muyaya. 10 Angati sitina chedwe, choonadi ziko tawi asembe ti baleko kuno kaci bili." 11 Atate babo Israeli ana kamba kwabeve, ngati cinkhala chocho, maje chitani ici. Tangani zabwino mulomuno mumasaka. Pelekani pasi kwa munthu uyu paso zina baimu ndi uchi. Zonukilisa ndi maya, pistachio nati ndi almondi. 12 Tengani dalama mupatikizapo mu manja yanu. Dalama ina bwe zalewa pamene muna segula masaka yanu. Zinyamuleni futi mumaja yanu. Kapena ana sokoneza. 13 Tenganiso mubale wanu. Nyamuka ndi ku yendaso kwa munthu uyu. 14 Lekani mulungu wamphamvu zonse akupaseni imwe chifundo pamaso ya munthu uyu, kwakuti akamulekeleko mubale wanu ndi Benjamani gati nafielewa mwana, na feleawa. 15 Anthu anatenga paso izi. Ndi mu manja yao antenhga zopatikiza muyeso wa dalama, pamozi ndi Benjamini. Ana nysmuka ndi kuyenda pasi ku Igipito ndi ana imilila kwa Yosefe. 16 Pamene Yosefe anaona Benjamini pamozi ano, a na kamba kuli osungila nyumba yake." Ba lete banthu munyumba, paya nyama ndi mpika daba banthu bazadya na ine muzuba. 17 Osunga zamunyumba ya Yosefe ana chita monga Yosefe akambila. Anabaleta kunyumba ya Yosefe. 18 Aba banthu ba nacita manta chifukwa bana pelekewa kunyumba ya yosefe. ba na kamba, " Ni chifukwa cha dalama yamene ina bwezelewa muma saka tawi yoyamba tina ikiliwa mukati. Kuti ati sakile mupata motisuza ife. Kuti ati mage ise ndi kutitenga akapolo ndi a bulu. 19 Ana mufikila osunga nyumba ya Yosefe ndi ku kamba naye po lobela munyumba, 20 anati bwana, koyamba ku gula vakudia. 21 Zinazinachika, pamene tina fika pamalo tina pumulila tina segula masaka yanthu, ndipo, onani, aliyese pamene tina segula masaka tathu dalama zake zina mumasaka yenze yo kwanila mupimo. tazi bwelesa mumaja yathu. 22 Dalama zina ndiposo tabwelesa mumaja yathu kugula vakudya. Citiziba wamene anti ikila mumasaka yathu." 23 Osungu anakamba. " Mutendele ukhale na inu. Musa yope. Mulungu wanu ndi Mulungu watate wanu anakufakila moni dalama zanu musaka yanu. Nina ladila dalama yanu." Osunga ana muleta simiyoni kwa beve. 24 Osunga anaba peleka amuna kunyumba ya Yosefe. Anaba pasa manzi, nidipo bana suka medo yabo. Ana pasa zakudya mabulu yao. 25 Bana kozekela paso za Yosefe kubwela kwake kwamu zuba, daba bana vela kuti zadiyela kuja. 26 Pamene Yosefe ata bwela kunyumba, ba naleta paso yamene yanali mumanja munyumba ndi kugwanda pansi. 27 Anaba fusa zaumoyo wao ndi ku kamba. " Ushe batate banu bali cabe bwino, ba chikulile ba mene muna kambapo? Kondi ali moyo?" 28 Bana kamba, " Wachito wanu atate batu bali bwino akali namoyo." Ndipo anamu gwadila kumu chitila ulemu. 29 Pamene ana nyamula menso yake ana ona Benjamini mu bale wake, mwana waba mao make mwamuna. Ndipo ana kamba, " Uyu dye mungono wake wamene una kambapo kuline?" Ndipo ana kamba. " Leka Mulungu aku chitile chisomo kwa iwe mwana wangu mwamuna." 30 Yosefe ana tamanga kuchoka muchibinda, daba china mukwila mutima kwabili kamba kabale wake ana sakila malo kwina kolilila ana enda ku chibinda chake ndi kulila. 31 Ana samba kumenso kwake ndi ku cho. Ana zi lesa eve, ku kamba kuti, " Ikani va kuya." 32 Wachito ana konza chakudya cha Yosefe kwa eyeka ndipo abale bake pa beka aku Igoipito ano anadya pabeba chifukwa aku Igipito sanali dyele mukate pamozi nama Hebeli. Kwa ici ni chonyesa ku banthu ba ku Igipito. 33 Abale bake ana nkhala pamaso pake Oyamba kubadwa kukonka mwamene bana badwila. Ndipo wa cicepele kuligana na uyamata wake anthu ana dabwisiwa chapamozi. 34 Yosefe anatuma mupimo wazakudia pa songolo pake. Koma Benjamini mupimo unali usanu kupabana a bale ake. Anamwa ndipo bana kondwela na eve.