Mutu 42

1 Ndipo Yakobo anaona kuti munali vakudya mu Egipito. Anakamba kuli bana bake bamuna. Cifukwa nichani muyang'ana yang'ana? 2 Anakamba, onani apa, namvera kuti kuli vakudya mu Egipito, Yendakoni kuti mukati gulile kuti tinkhale namoyo tisamwalile. 3 Abale bake ba Yosefe bali banayenda kugula vakudya ku Egipito. 4 Koma Yakobo sana tume benjamini, mubale wake wa yosefe, pamozi na bale bale popeza anakamba kuti, "Niyopa kuti voipa vingacitike pali yeve. 5 Bana ba Israyeli banabwera kugura pakati kabaja banabwera, cifuka njala inali mu ziko ya Kanani. 6 Ndipo Yosefe anali bolamulila ziko. Ndipo anali kugulisa kubanthu bonse ba muziko. Abale bake ba Yosefe banafika nakubelama pansi na nkhope zao pansi. 7 Yosefe anaona babele bake nakubaziba ana zibisi kuli beve naku kamba nabo mo limba anakamba nao, mwacokela kuti? Banakamba kuli tacokela ku Kanani kubwela kugula vo kudya. 8 Yosefe anabaziba ba bale bake, koma beve sibana muzibe. 9 Ndipo Yosefe anakumbuka viloto vamene analota pali beve, anakamba nabeve kuti, ndimeneo oipa mwabwela kuona mbali zamene zilibe citezo mu ziko. 10 " Anakamba kuli yeve kuti, awe mbuye wanga. Ba kapolo bako babwla kugula vakudya. 11 Ndise bana bamunthu umozi tonse, ndife banthu bazoona, bakapolo bako si banthu oipa. 12 Anakamaba nao kuti, "Awe, mwabwela kuona malo mulibe citeyezo mu ziko 13 Bana kamba kuti, "Ife akapolo bako tili abale tyovu, bana bamunthu umozi muziko ya kenani. Ona, mufuna maningi lelo ali nabatate bathu na mubale wathu umozi salimoyo." 14 Yosefe anababuza kuti, "Ndiye vamene naku uzani. ndimwe oipa. 15 Pali ici muza yesewa na moyo wa falabo, simuzacoka pario, koma cabe ngati mubale wanu mung'onu abwere kuno. 16 Tmani umozi mumusiye akatenge mubale wanu. Muzasala mundende, kuti mau yanu yayesewe. Kuona ngati muli cazo ona muli imwe. Ngati siivo, pa moyo wa Falao ndimwe oipa zo ona. 17 Anaika bonse mundende musiku yatatu. 18 Yosefe anakamba nabeve pasiku yacitatu, " Citani ici kuti mukhale namoyo, Popeza niyopa Mulungu. 19 Ngati ndimwe bamuna bazo ona, lekani umozi wa abale wanu akhale mundende iyi, koma imwe mu yende, nyamulani vokodya vanjala ya manyumba yanu. 20 Bwelesani mufana wanu kuti mau yanu ya simikiziwe ndipo simuza mwalila." Ndio banacita zimezo 21 Banakambisana wina na muzake, " tinachimwila mubale wathu pakuti tina ona ,kutika kwa moyo wake pamene ana papata kuli ife pamene. anati pempha ndipo sitinamvela, cifukwa caici mavuto yatifikila. cifukwa caici mvuto yatikila. 22 Rubene anabayankha, "KOdi sina kuuzane, Osamucimwila munyamata! Koma sina mvele? Manje onani, magazi yake ya funika kwa ife." 23 Sabanazibe kuti Yosefe anabamwesesa, cifukwa panali omasulila pakati kao. 24 Anacoka pali beve ndipo analila. Ana bwelela kuli beve nokamba nao. Anatenga simiyoni nakumu manga menso yao. 25 Yosefe ana lamulila ba nchito bake kuti ba zuze machola na vakudya, ndikuika ndalama za munthu alibonse mucola cake, ndi ku bapasa vose vofunika paulendo. zinacitika. 26 Abale anasenzesa Abulu ao vakudyandi kuyambapo. 27 Pamene umozi anasegula saka kuti apase bulu zakudya mu malo yopumulila, ana ona ndalama zake. Taonani zinali muku segula kwa thumba yake. 28 Anakamba kuli abale ake, " Ndalama zanga za bwezewamo, zioneni, zili mutumba yanga, "Mitima yanamila anapindamuka monjemela kuyanganana wina na mzake, kukamba kuti, "Nicani ici camene Mulungu acita kuli ise?" 29 Anayenda kwa Yakobo, tate wo muziko ya Kanani ndi kumu uza vonse vinaba citikila. Banakamba kuti. 30 Munthu, mbuye waziko, an anakamba, naise moka lipo nakuti ona monga ndise oipa muziko. 31 Takamba kuli yeve, ndife bamuna bazona, sindife boipa. 32 Tili abale tyovu, bana ba atate bathu, umozi salimoyo, ndipo ndipo mung'ona lelo ati na batate muziko ya Kenani. 33 Munthoyo, mwine ziko, anakamba naise, kupitila muli ici nizaziba kuti ndimwe amuna bazo ona. Siyani mubale wanu umozi naine,, tengani vakudya ya njala ku manyumba yanu, ndipo yambaponi. 34 Bwelesani mufana wanu maningi kuli ine. Ndipo nizaziba kuti sindimwe oipa, koma kuti ndimwe bamuna bazoona, Pamenepo ndizatulusa mubale wanu, ndipo muzagulisa muziko." 35 Vinacita pamene anasegula matumba yao kuti, taonani, thumba yalionse munali siliva. Pamene beve naba tate bao banaona mutumba ya siliva, banayopa. 36 Yakobo tate wao anakamba kuli beve, "Mwanitengela bana banga, Yosefe salimoyo, Simioni naye ayenda, ndipo mufuna kutenga Benjamini. Vonse ivi vinthu vaninyamukila ine." 37 Rubene anakamba naba tate bake, kuti, mungapaye bana banga babili ngati siniza bwelesa Benjamini kuli imwe, muakeni mumanja yanga, ndipo ndizaleta kuli imwe futi." 38 Yakobo anati, "Mwana wanga mwamuna sazayenda naiwe, popeza mubale wake anafa ndipo anasala yeka. Ngati voipa vizabwela pali yeve munjira yamene muyendamo, ndipo muzaleta imvi zanga ndicisoni kumanda.