Mutu 4

1 Mwamuna anaziba Eva mjukazi wake ndipo anankala na pakati naku bala Kaini. Eva anakamba, "Nabala mwana mwamuna na tandizo ya Yehova." 2 Ndipo ana bala mubale wake Abelo. Manji Abelo anankala mu busa koma Kaini ulima mu munda. 3 Vinachitika mukayenda kwa nthawi Kaini analete vipaso vamu munda mongo vopeleka kwa Yehova. 4 Koma abelo, analeteko nyama zoyambila kubadwa pali nyama zake na mafuta. Yehova anavomela Abelo na vopalike vake. 5 Koma Kaini no vopeleka vake sina vomele. Ndipo Kaini ana kalipa maningi, naku khumundwa. 6 Yoheva aba uza Kaini, "Nichifukwa chani wakalipa naku khumundwa? 7 Ngati wa chita cha bwino siuza vomelewa? koma ngati siuna chite chabwino uchimo ugogoda pa chiseko ufuna kuku lamulila, koma ufunika ku ugonjesa." 8 Kaini ana kamba na Abelo mu bale wake. Zinachika kuti pamene banali mu minda Kaini anaukila mubale wake naku mupaya. 9 Ndipo Yehova anafunsa Kaini, "Alikuti Abelo nubale wako?" Anakamba, "Sinniziba. Nanga ndine malonda wake?" 10 Yehova akamba, "Nicani chame wachita?" magadzi ya mubale wake yanililila kuchoka pansi. 11 Manje wa tembelelewa ku xhokela pansi, pamene pasegula kwamwa kakekulandila muhadzi ya mubale wako kuchoka ku kwanja yako. 12 Uka lima munda, kucho manje apa siuzakupasa kuchola mumpavu yake uzankhala othaba mulandu na oyendayenda. 13 Kaini anakamba kuli Yehova, "Chilango changa chakulisa pitilila vamene ningakwanise. 14 Zoona, mwanipitikitsa pa siku ya lelo mu munda uno, ndipo niza bisiwa pa menso panu. Niza nkhala utaba mulandu na oyendayenda mu chalo, na aliyense azanipeza ozani paya ine." 15 Yehova anamuuza, "Ngati aliyense aza paya kaini; azabweseewa kasano ndi kabili." Ndipo Yehova anayika chizindikilo pali Kaini kuti ngati aliyense amupedza, uyo muthu si azamu menya. 16 Ndipo Kaini anchoka pa manso ya Yehova naku nkhala kumalo ya Nodi; ku mawa kwa Edeni. 17 Kaini ana ziba mukazi wake nakunkhala na pakati. Anabala Enoki. Anamanga muzi nakuii pasa zina ya mwna wake Enoki mwamuna. 18 Kuli Enoki kuna badwa Iradi. Iradi anankhala tate wa Mehujeli. Mehujeli anakhala tate wa Methusheli. Methusheli anankhala tate wa Lamekhi. 19 Lamekhi ana kwatila ba kadzi babili. zina yamukadzi umodzi inali Ada, na zina yamukadzi wina inali Zilla. 20 Aada ana bala Jabala. Anali tate wa wonse banali kunkhala muma hema bamene banali na Zobeta. 21 Zina yamu bale inali Jubala. Anali tate wa bonse bame amalidza zilimba. 22 Koma Zila ana bala Tubala-kaini, opanga Zisulo za munyala ya blonze no nsimbi. Mulongosi wa Tubala-Kaini anali Nama. 23 Lamekhi ana uza bakadzi wake, "Ada na Zila nvelani mau yanga; imwe akadzi ba lamekhi, nelani vamene nikambe. Chifukwa napaya munthu ndaba anipanga chilonda ine, munyamata pakuti myula ine. 24 Ngati Kaini banamubwezela kasano nathibili, ndipo lamekhi azabwezelawa kokwanila sevente seveni. 25 Adamu ana Ziba mukadzi wake nafuti, ndipo mukadzi wake abala mwana wina mwamuna. Anamu pasa zina yakuti Seti nakukamba kuti, "Mulungu anipasa mwana mwamuna winangu pamalo ya Abelo, chifukwa Kaini anamu paya." 26 Mwana mwamuna anabadwa kuli Seti amanupasa dzina yakuti Enosi. Panthawi iyo banthu banayamba kuyitana pa dzina ya Yehova.