Mutu 39

1 Yosefe ana letewa ku Egipito. Potifa, mu sogoleli wa Farao wamene anali muklu wama malonde waku Egipito, anamu gula kuli ma Ishmaelites, wamene anamaleta kuja. 2 Yehova anali na Yosefa ndipo ana nkala olemela kwambili. Ana nkala mu njumba ya bwana wake waku Egipito. 3 Abwana bake bana ona kuti Yehova anali na Yosefe na zonse zamene anali kuchita yehova ana chulukisa. 4 Yosefe anapeza mwai. Anamu sebezela Potifa. Potifa anapanga Yosefe bwana wapa nyumba yake, navonse vintu vake, anavi ika mu manja mwake. 5 Zina chitika kuti choka pamene ana nkhala musogoleli wapa nyumba na vonse vintu, Yehova anadalisa nyumaba yawaku Egipito chifukwa cha yosefa. Daliso ya Yehova inali na vonse vintu va Potifa vamu nyumba namu munda. 6 Potifa ana ika vonse vintu vake mumanja ya Yosefa. Sanali kufunika ku ganiza pali chili chonse koma chabe chokunya chamene eze kudya. Ndipo Yosefa anali wa bwino nakuoneka bwino. 7 Zina chitika ku choka apa kuti mukazi wa bwana wake anamu kumbwila Yosefe no kamba, " Gona na ine." 8 Koma anakana ku gona naba kazi ba abwana bake, " Ona, bwan wanga sama ikako nzelu ku vonse nichita mu nyumba yabo, anani ika ku langanila vonse vintu vabo. 9 Kulibe mwamukulu mu nyumba muna pali ine sana bisa kantu kuli ine koma iwe, chifukwa ndiwe mukazi wake. Ninga chite bwanji zo ipa izi naku chimwila Mulungu?" 10 Anakamba na Yosefa siku na siku, koma anakana ku ngona nabo olo ku nkala naye. 11 Zina chitika kuti siku imozi anayenda ku sebenza ku nyumba. Amuna bonse sibana liko mu nyumba. 12 Anamu gwila pa chovela naku kamba, " Gona na ine." Anasiya chovala mu manje yake, kutaba, kuyenda panja. 13 Ina bwela kuti, pamene anaona kuti psaya chovala mu manja naku tabila panja, 14 ana itana amuna ku nyumba naku bauza kuti, " Ona, Potifa ati letela muntu wachi Hebeli kuti sobelesa. Ezeli abwela kuti agone na ine ndipo napunda. 15 Zinaditika pamene napunda, ataba kusiya chovala naine, nakuyenda panja." 16 Ana ika chovala chake pafupi na eve mpaka ba bwana bake ba bwela ku nyumba. 17 Anamu londolela izi, " Mu Hebeli wa nchito wamene unaleta kuli ise, eze abwela kuni sobelesa. 18 Zabwela za chitika kuti pamene napunda, ataba kusiya chovala chake naine, atabila panja." 19 China chitika, pamene abwana ana vela ku londolola kwaba kazi abo, " Ichi ndiye chamene wa nchito wako achita kuli ine," Ana kalipa kwambili. 20 Abwana ba Yosefa banamutenga naku ika mu ndende, mu malo mwamene akaidi ba mfumu banali. Ezeli mu ndende. 21 Koma Yehova anali na Yosefa nakumu onese ku kulupilika kwachi pangano. Anamu pasa mwai mu menso yao olonda ndende. 22 Olonda ndende ana pasa mu manja mwa Yosefe bonse akaidi banali u ndende. Vilivonse vamene bana chita kuja, Yosefe anali oyanganila. 23 Olonda ndende sanade nkawa pali chili chonse chinali mu manja yake, chifukwa Yehova anali na eve. Zili zonse zamene ana chita, Yehova ana chulukusa.