Mutu 38

1 Inabwela ntawi pomwe Yuda anasiya abale bake nonkhala kuli omwe anali na zina la Hira. 2 Anapeza kuja mwana mukazi wa mwamuna waku Kenaani anali na zina la Shuwa. Anamutenga ndipo anamungela. 3 Anankhala na mimba na bala mwana mwamuna. Anamupasa zina la Eri. 4 Anankhala na mimba nafuti nomabala mwana mwamuna. Anamupasa zina la Onani. 5 Anankhala na mwana mwamuna nafuti nomupasa zina Sela. Kunali ku Kezib kwe anamubalila. 6 Yuda anapezela Eri mwana wake woyambilila, mukazi wo kwatila zina lake anali Tama. Eri, mwana wa 7 Yuda wo yamba, analiuchita zo chimwa pa menso ya Yehova. Yehova anamupaya. 8 Yuda anati kuli Onani, "ngenela mukazi wa Abbale bako. Chita nchito yamulamu mwamuna kuli eve, kuti ukulise mwana wamu abale bako. 9 Onani anaziba kuti bana zibaza nkhala bake. Lyonse akangena kumukazi wamu bale wake, anatila pansi mpavu vachimuna kuti anankhale na mwana wa abale ake. 10 Ve anachita venze vochimwisa pa menso ya Yehova, Yehova anamupaya na eve. 11 yuda anati kuli Tama, muoungozi wake, "Upitise kunkhala wofesdwa munyumba yabatate bako kafika sela, mwana wanga, akakule."chifukwa anayopa, " Kuti angafe nayeve, monga abale bake." Tama ayenda kunkhala munyumba yabatate bake. 12 Patapita ntawi itali, mwana mukazi wa Shua, mukazi wa Yuda, anafa. Yuda bana mutontoza ndipo anayenda kuli bo embela mbelele zake ku Tina , eve namukaze Hira waku Adulamayiti. 13 Tama bana muwuza, "wona, ba pongozi bako bamuna bayenda ku Tina kuyembela mbelele zake." 14 Anachosa zovala zamukazi wafedwa ndipo anazivwinikila na nyula nozimanga. anakhala pongenela mumalo ya Enami , inali pambali pa njila yaku Tina. chifukwa anawona kuti Sela akula koma sibanamukwatilise kuli eve. 15 Pamene Yuda anamuwona anaganiza monga nimukazi wachiwele wele chifukwa enze anabisa nkope yake. 16 Anyenda kuli eve ndipo anti, "Bwela, leka naiwe chifukwa sana zibe kuti nimupongozi wake mukazi ndipo mukazi anakamba kuti, "Uzani pasa chani ukagona naine?" 17 Mwamuna anakamba kuti, "Niza kutumila kambuzi kang'ono kuchoka kuzobeta." mukazi anakamba kuti, "uzampasa lowezo kufikila ukatume?" 18 Mwamuna anakamba kuti, "Nilonjezo bwanji yeningakupase? mukazi anayanka, "chidindo na ntambo yako na ndondo ili mumanja yako."Anamupasa no yenda kuli eve, ndipo anankhala na mimba yake. 19 Mukazi anayima noyenda njila yake. Anachosa nyula yake no vala zovala za wofedwa. 20 Yuda anatumiza ka mbuzi kang'ono kupitiula mumunzake waku Adulamiyiti kuyi angetenge lonjezo lake kuchokela mumanja yamukazi, kuno sanamupeze. 21 Waku adulamayiti anafunsa ba muna ba pa malo, "alikuti mukazi wachiwelwwele enze pa mbali pa njila ya Enami?" Banakamba kuti."kunalibe mukazi wachiwelwbwele pano." 22 Anabwele kuli Yuda anakamba kuti, "Sinamupeze. Nabamuna ba pamalo banakamba kuti, 'kuliba mukazi wechiwelewele pano." 23 Yuda anakamba kuti, mutekeni usunge vintu, kuti tisaletelewe nsoni, chifukwa, nonatuma ka mbuzi kang'ono koma sunamupeze." 24 Pekunapita myezi itatu uda banamuza kuti. "Tama mupongozi wako mukazi achita zawewelele, ndipo anankhala mimba. "Yuda anakamba kuti, "Muleteni kuno timushoke." 25 Pabanamuleta panja, anatuma utenga kuli bapongozi bake, "Nilinamimba ya mwamuna alina vintu ivi." Mukazi anakamba kuti, "Sakilani mwine wa ivi, chofundo na ntambo na ndondo." 26 Yuda anaviziba no kamba kuti, "Niwolungama kuchila ine. chifukwa sinina mukwatolise ku mwna wanga, Sela." 27 Pamene inafika ntawi yonkala na mwana, Onani, bampundu banli mumala. 28 Inafika pamene eze ku bala umozi anachosa kwanja panja, ndipo wabalisa anatenga ka ntambo ka redo no kamanga pa kwanja nokamba kuti, "Uyu ayambilila kuchoka." 29 Koma pamene ana bweza kwanja, ndipo, Onani, bale wake anayambilila kuchoka. Wobalisa anakamba kuti, "Mwewachokela!" Ndipo bana mwitana kuti Perezi. 30 Bale wake anachika, anali naka ntambo ka redi pa kwanja, ndipo bana mwitana kuti Zera.