Mutu 32

1 Naye Yakobo anayenda njila yake naba ngelo ba Mulungu bana mukumanya iye. 2 Pamene Yakobo ana one, "anakamba iyi i hema ya Mulungu." ana itana zina yayaja malo mahanayimu. 3 Yakobo ana tuma atumikila kusogolo kwake kuli mubale wake Esau mumalo yaseya, mu malo ya Edomu. 4 Anabalamulila kukamba, Izi ndiye zamene uzakamba kuli mbuye wanga Esau. Ichi ndiye chamena akamba Yakobo kapolo kwanga kufika lelo. 5 Nili ng' ombe na abuvu. na vaweta naba nchito bamuna na bakazi. Natuma aya mau kuli abwna banga kuti apeze mwai mu menso yako. 6 A mithenga banabwela kwa Yakobo ndipo anati, "Tina yenda kuona mubale wako Esau. Abwela kuzakumana naiwe, nabamuna bali fihandredi bali nayeve. 7 Ndipo Yakobo anayopa na kukwiya. Ndipo anagaba banthu bamene enze mumagulu yabili, na vobetaa, ng' ombe, ndi mabulu. 8 Anakamba kuti, "Ngati Esau abwela kugulu imozi ndi kuimenya, ndipo gulu yamene izasala izathaba. 9 yakobo anati, "Mulungu wa atate banga Abrahamu, ndi Mulungu wa batate banga Isaki, Yehova anakamba kwa ine, Bwelela ku ziko lako ndi kwa abale ako ndiponizakupeleka pasongolo. 10 Sindine oyenela pali vonse vocita vacipangano co kholulupilila ndi zabwino 11 Napapata ni pulumuseni ku kwanja yu mu bale wanga, ku kwanja kwa Esau, chifukwa nili na mantha kuti azabwele ndi kundimenya ndi bazimai nabana. 12 Koma wakamba kuti, "Nizakupanga kuti utukuke nizapanga bana bako monga dohti ya munyanja, yamene singabelengeke mu ma nambala. 13 Yakobo anakhamba uja usiku uja. Anatenga vina enze navo monga mphaso kuli Esau, mubale wake. 14 Mbuzi zikazi zili thu handiledi ndi mbuzi zimuna zili twenti, nkhosa zikazi zili thuhandiledi, ndi nkhosa zimuna twenti. 15 Ngamila zamkaka zili feti na tu bana twao. Ng'ombe zikazi zili fote, na ng'ombe zimuna zili teni, mabulu yakazi yali twenti ndi ma bulu yamuna yali tenni. 16 Ivi anapasa mumanja nwa ba nchito bake, gulu payekha yeke, anakamba kuli ba nchito, "Pitani kusogolo kwanga ndipo muike mupata pakati panagulu. 17 Aba uza wa nchito woyamba kuti, pamene Esau mubale wanga akumana naiwe na kukufunsa, kukamba, ili kumbali yandani? Upita kuti? ni nyama zandani izi zili kusogolo kwako? 18 Ndipo uza kamba kuti, 'ndiwa nchito wako Yokobo ndi mphaso yatumi ziwa kuli bwana wanga Esau. Ona, naye alikubwela mumbuyo mwathu. 19 Yakobo anapasanso malamulo gulu lacibili, lacitatu, ndi amuna onse ana konka, ng' ombe. Anakamba, muzakamba vinthu vimozi mu kakumana ndu Esau. 20 Mufunika kukamba wa nchito wako Yakobo abwela pambuyo, "Cifukwa anaganiza," nizamu kondwelesa iye na mphaso zamene nituma kusogolo kwanga pambuyo pake, nikamu ona paena azandi landila ine. 21 Mphaso zina yendelatu ku sogolo kwake.Iye usiku uja anakhala mu hema. 22 Yakobo anauka usiku ndipo anatenga bakazi bake babili, banchito bake babili bazimai, nabana bake bamuna levini, anabatuma kutauka pa abokola Yabboki. 23 Munjila iye anabatuma kutauka mumana na cuma cao conse. 24 Taboko anasijiwa yeka, ndipo analimbana na munthu pakana kunaca. 25 Pamene uja munthu anaona kuti sinizamkwanisa, anaonga nchafuyake, nchafu ya Yakobo inasinthani pamene banali kulimbana. 26 Munthu uja anakamba, nisiye, apeza kwayamba kucha, "Yakobo anakamba, "Sinizakuleka pakana unidalise. 27 Munthu anakamba kuli yeve, "Zina yako ndiwe ndani? Yakobo anati, "Yakobo." 28 Munthu anakamba, zina yako sizkhlnso Yakobo koma Israeli. Chifukwa walimbana ndi Mulungu ndi banthu koma wa pambana. 29 yakobo anafunsa, "Napapata niuze zina yako? Anati, "Ufunsila chani zina yanga? ndipo anamusalisa paja. 30 Yakobo anaitana pamalo paja kuti peniwenlo popeza anti, naona Mulungu menso na menso ndipo moyo wanga wapulumuka. 31 Zuba inacoka pamena Yakobo anadusa peniwelo anali ku golontha chifukwa ca achafu yake. 32 Ndiye chifukwa cake kufika nalelo banthu ba ku israeli si kudya nyama zamene zipezeka pafupi nanchafu cifukwa munthu ana onanga zibalo pa ku siyanisa nchafu Yakobo.