Mutu 31

1 Ndipo Yakobo anamva mau ya bana ba Labani, yamene banakamba, "Yakobo atenga vonse va batate bathu, apeza chuma conse ici kuckela mu vinthu va batate. 2 Yacobo anaona kayang'anidwe pa menso pa Laban. Anaona kayang'anidwe kake kanacinja. 3 Ndipo anatuma ndi kuitana Rakele ndi bwelala kuziko ya batate bako na ba bale bako ndipo nizankhala naiwe. 4 Yacobo anatuma ndi kuitana Rakele ndi Leya kui abwele kumunda kuli zobeta zake. 5 Ndipo anakamba na beve, "Naona kayanganidwe kaba tate banu pali ine kacinja, koma Mulungu wa tate ali naine. 6 Muziba kuti na mpavu zanga zonse nankhala nisebenzela batate banu. 7 Batate banu baninama na kucinja malipilo yanga kali 10, koma Mulungu sana muvomeka kucita coipa. 8 Ngati anakamba kuti, nyama za manthongo ndiye malipiro yako, 'ndipo zonse nyama zinabala zamanthongo, ngati akamba kuti, zamizela zizakhala malipiro yako, ' ndipo nyama zonse zinabala zamizera. 9 Cifukwa cake Mulungu anatenga nyama za batate banu na ni pasa. 10 ndipo pa nthawi yobala, ninaona muciloto mbuzi zimuna zinali kukwela nyama. Mbuzi zimuna zinali namizela, na mamphongo na mitundu yosiyana-siyana. 11 Mungelo wa Mulungu anakamba na ine mu ciloto, 'Yakobo' ninakamba, 'nili pano.' 12 Anakamba kuti, nyamula menso yako ndipo uone mbuzi zonse zimuna zikwelana na nyama. Zinamizela mamphongo, na mitundu yosina-siyana, cifukwa naona vonse vamene Labani acita kuli iwe. Ndine 13 Mulungu wa Betele, kwamene unathila mafuta pamwala, kwamene unalumbila kuli ine. Manje nyamuka ucoke m'malo yano na kubwelela kumalo kwamene unabdwila." 14 Rakele na Leya anayankha na kukamba na eve, nanga kulibe mbali na vosalila vathu munyumba ya batate? 15 Sitisungiwa na eve monga ni balendo?cifukwa atigulisa nakuonongeltu nadalama zathu. 16 Pa cuma ciliconse camene bacosako kuli batate bathu cankhala cathu na bana bathu. Manje, vilivonse vamene Mulungu akamba, cita." 17 Ndipo Yakobo ananyamuka noika bana bake bamuna na bazikazi bake pa ma bulu. 18 Anaika zobeta zake pa songolo pake, pamozi nakatundu wake bonse, kuikilapo nanyama za mene anakhala nazo mu paddani Aramu. Ndipo anakonzekera kuyenda kuli Isaki tate wake mumalo yao ya Kanaani. 19 Pamene Labani anayenda kukasenga nkhosa zake, Rakele anaba tumilungu twa munyuma ya batate bake. 20 Yakobo ana namanso Labani wa ku Aramean, po samu uza ati ayenda. 21 Ndipo anathaba na vonse enze navo na kudusa pa mumana, ndipo anayendela ku phili yaziko ku Giliyadi. 22 Pasiku ya citatu Labani ana uziwa kuti Yakobo anathaba. 23 Ndipo anatenga abale ake ndi kumupisha kwa ulendo wamasiku seveni. Anamupeza pa phiri ya ziko ya ku Giliyadi. 24 Ndipo Mulungu anabwera kwa Labala mu Aramean muciloto naku mu uza kuti, "Nkhala ocenjera kuti osakambe voipa olo vabwino kuli Yakobo. 25 "Labani anapitilila Yakobo. Ndipo Yakobo anamanga hema yake mupili yaziko. Labani naye anakhala paja mba bale bake mupili ya Giliyadi. 26 Ndipo Labani anakamba kuli Yakobo, wacita cani, kuti unani nama nakunyamula bana banga bakazi monga ba kaida ba nkhondo? 27 Cifukwa nicani unathaba mwacisinsi na kuninama ndiponso sunani uze ine? Asembe nina kupelekeza nakusangalala na nyimbo, ndi lingaka ndi coliza. 28 Sunandi vomekeze ine ku mpsompsona bana banga bakazi na bamuna, manje wacita vopusa. 29 Vili mu mphavu zanga kukucita voipa, koma Mulungu waba tate bako anakamba usiku wasila ndipo anati, 'Khala wocenjela, kuti osakambe kuli Yakobo voipa na vabwino.' 30 Manje wayenda cifukwa wenze kufuna maningi kubwelela kunyumba ya batate bako. Nanga nichani camene unabela milungu yanga?" 31 Yakobo anayankha nanena kwa Labani, "Chifukwa ninayopa nakuganiza kuti muzapoka bana banu bakazi mwampavu ndaba sinilaile. 32 Alionse wamene aba milungu yanu saza pitiliza kukhala na moyo. Pamenso ya ba bale bathu, ona cili conse cili naise ngati nichanu mucitenge. "Cifukwa Yakobo sanazibe kuti Rakele ndiye anaba. 33 Labani anangena muhema ya Yakobo, na muhema ya Leya, ndiponso muhema ya banchito babili, koma sanaba peza. Anocoka muhema ya Leya na ku ngena muhema ya Rakele. 34 Ndipo Rakele anali anatenga milungu zamunyumba, anaviika pa conkhalila caca ngamila, ndi kunkhalapo. Labani anasakila muhema yonse, koma sana vipeza. 35 Anakamba kuli atate bake, "Osakalipa, mbuye wanga, kuti siningamilile pamenso pano, cifukwwwa nili panthawi ya kumwezi. "Ndipo anasakila koma sana peza milungu za munyumaba mwake. 36 Yakobo anakalipa naku kangana na Labani. Anakamba kwa iye, "Kodi mulandu wanga ndiwa bwanji?Cimo yanga niya bwanji, kuti muzingo kuni konka konka? 37 Popeza mwa sukila ponge pali katundu yanga. Nichani came mwapeza pavinthu vonse va munyumba yanu? Vileteni apa pali abale athu, kuti ba weruzu pakati ka ife. 38 Kwazakatwenti na nkhala naimwe. Nkhosa zanu nambuzi zikazi sizina kangangepo kubala, olo kapena kudyapo pa vo beta vako. 39 Vina vina ng,ambiwa na vilombo sinina vilete kuli iwe, koma, ndine ninalipila pava mene vinasowa. Nthawi zonse mumanindi pilisa pali nyama yadoba, loko yabewa usiku olo muzuba. 40 Ndipo nenzeko, musiku zuba inani shoka, mame ya usiku ndipo sinina gone usiku. 41 Izi zake twenti nankhala munyumba yako, nina kusebenzela iwe zaka fotini cifukwa ca bana bako babili bakazi, nazaka sikisi vobeta vako. Mwacinja malipilo kali teni. 42 Pokhapo Mulungu wa batate banga, Mulungu wa Abrahamu ndi iye wamene kaki ayopa, anali na ine, zo ona mwenze kuti niyende popanda vilivonse mu manja mwanga. Mulungu ayangana kuvutika kwanga na mwamene nenze kusebenzera maningi, ndipo anaku kalipila busiku wayenda." 43 Labani anayankha na ku kamba kuli Yakobo, "Akazi aba ndiye bana banga bakazi, bazukulu niba zukulu bangaa, navobeta ni vobeta vanga. vonse vamene uona nivanga. Koma nichani lelo ninga cite kuli aba banga bakazi kapene bana bao bamene bana bala? 44 Manje apa, tiye tipange cipangano, iwe naine,ndipo ndiye ciza nkhala kamboni pakati ka iwe na ine." 45 Ndipo Yakobo anatenga mwala nakuika pamwamba pa pila. 46 Yakobo anakamba kuli babale bake, "Ikani miyala pamozi," ndipo banatenga miyala nakuzi bunjika. Ndipo banadyela pamwamba. 47 Labani ana itanapo Jegara saha Duthu, koma Yakobo anaitanapo Gilayadi. 48 Labani anakamba, izi miyala ni kamboni pakati kaiwe naine, lelo "Cifukwa cake zina yake baitanapo Giliyadi. 49 Paitaniwanso mizipa cifukwa Labani anakamba, Leka Yehova ayangane pakati kaiwe na ine, pamene tisiyana wina na muzake. 50 Ngati suzasunga bana banga bakazi bwino, olo uzatenga bakazi bena pambali ya bana banga bakazi, loko palibe wina ali naise, ona, Mulungu ni kamboni pakati kaiwe na ine." 51 Labani anakamba kuli Yakobo, " Yangana pamwamba, ndipo ona pa pila, yamene naika pakati kaiwe naine. 52 Iyi nthutu ndiye kamboni, na pila ni kamboni kuti sinaza jumpa iyi nthutu kubwera kuli iwe, ndipo na iwe suza jumpa iyi nthutu ku bwela kuli ine, kucita voipa. 53 Leka Mulungu wa Abrahamu, na Mulungu wa Nahor, na milungu za ba tate bao, ziweruza pakati kathu." Ndipo Yakobo analapa pakuyopa batate bake Isaki. 54 Yakobo ana peleka nsembe pa phiri nakuitana abale bake kuti bazadye cakudya. Ba nadya na kunkhala busiku bonse pamwamba pa lupili. 55 mumawa, Labani anauka, naku myompyona bazulu bake na bana bake bakazi na kubadalisa. Pamene Labani anacokapo nakubwelera kunyumba.