Mutu 25

1 Abrahamu a natenga mkazi wina, zina yake enze Keturah. 2 Ndipo anambalira iye Zimirani, Yokisani, Medeni, Midiyani, Isibaki ndi Suwa. 3 Ndipo Yokisani anakhala taet wa Sheba na Dedani, bana ba Dedani banali ba Assyriarl, ndi Letosu, ndi Leum. 4 Bana ba Midian bamuna benze Ephari, Epheri, Harlok, Abida, na Eldaah, bonse aba benze bana ba Ketura. 5 Abrahamu anapasa Isaki vinthu vake vonse. 6 Koma pene enze namoyo, anapasa mphaso bana bamuna ba bakazi bake bang'ono naku batuma kuziko la kumawa, kubacosa kuli Isaki, mwana wake. 7 Aya ndiye yannali masiku yazaka zimene Abrahamu anakhala namoyo, zake 175. 8 Abrahamu anapema kosiliza ana walila nazaka zabwino zokolamba, munthu nkhote namoyo okwana, anatengewa kuli banthu bake. 9 Isaki na Ishumaele bana bake, bana muika mumphanga isa makipela mu munda wa Ephrori mwana wa zohari mu hitati, yamene iri pafupi na mamure. 10 Munda wamene Abrahamu enze anangula kuli bana ba Heti. Ndiye Abrahamu na mkazi wake Sara banai kiwa. 11 Pambuyo paimfa ya Abrahamu, mulungu anadalisa mwana wake Isaki, ndipo Isaki enze kunkhala pafupi na Beeri Lahai Roi. 12 Ndipo aba ndiye benze bana ba Ishumaele, mwana wa Abrahamu yamene Hagara mu Egipito, kapolo wa Sara, anabalira Abrahamu. 13 Aya ndiye ynze mazina ya bana ba bamuna ba Ishumaele kulingana namwamene banabadwira: Nabioti woyamba wa Ishumaeli, Kedar, Adbeel, Mibsam, 14 Mishma, Duma, na MAsa, 15 na Hadad, Tema, Jetur, Naphish, na Kedemah. 16 Aba ndiye benze bana ba Ishumaele, ndipo ndiye yenze mazina yao, kulingana na mizi yao na misasa zao; akalonga 12 kulingana na mitundu yao. 17 Izi ndiye zaka zamoyo wa Ishumaele, zaka 137, ndipo iye anamwalira, ndipo anatengawa kuli bathu bake. 18 Ndipo banakhala, kuyambira ku Havilah na kufika ku Ashhuri, yamene ili pafupi na Egipito, monga iyenda ku Assirila. bankhala boyambana bekha bekha. 19 Ivi ndiye venze vocitika va Isaki, mwana wa Abrahamu, Abahamu ana bala Isaki. 20 Isaki enzeli na zaka 40 pamene kwatira mkazi wake Rabeka, mwana wa Betuero mu Aramearl wa ku Paddors Arars, Mlongo wake wa Labari mu Aramearl. 21 Isaki anapemphelera mkazi wake kwa Tehova cifukwa senze kubala, ndipo Yehova anayankha pemphero yake,ndipo mkazi wake Rabekah anakhala navumo. 22 Bana banavutana muvumo mwake , ndipo anakamba kuti, " Cifukwa ni chani ivi vicitika kuli ine?" Ndipo anayenda kufusa Yehova pali ivi. 23 Yehova anakamba nayeve, " Maziko yabili yali mu vumo mwako, Mangulu yabili ya banthu ya zachoka muli iwe, gulu izakhala ya mphavu kucila inzake, ndipo mkulu azakhala kapolo wa mufana." 24 Pamene nthawi yobala inakwana, Taonani, mwenze ba mpundu mu vumo. 25 Mwana woyamba anacoka wofiila monse monga chovala camasaku, ndipo ana mupasa zina yake Esau. 26 Pambuyo pake mubale wake anacoka, kwanja kwake kunagwira kadenene ka Esau. Anapasiwa zina ya Yakoba. Isaki enze nazaka 60 pamene mkazi wake anabala. 27 Ndipo banyamata banakula, ndipo Esau anakhala oziba kusakira nyama, munthu wa msanga. Koma Yakobo enze munthu wa zii, wamene enze kukhala mumatenthi. 28 Ndipo Isaki anakonda Esau cifukwa anadya nyama zamene anasakira, koma Rabekah anakonda Yakobo. 29 Ndipo yakobo anaphika supu, Esau anabwera kucoka kusanga, analema nanjala. 30 Esau anakamba na Yakobo ati, " Nipaseko supu yofilla napapata nalema!" Ndiye cifukwa zina yake enze Edomu. 31 Yakobo anakamba kuti, " Coyamba unigulise ukulu wako," 32 Esau anati ona nili pafupi nokufa, ukulu uli nanchito bwanji kuli ine? 33 Yakobo anakamba kuti, " Yambira kulumbirira kuli ine" Ndipo Esau analumbila njazi ndipo mnjira iyo anagulisa ukulu waka ku Yakobo. 34 Yakobo anapasa Esau mkate na supu yo phika, ndipo anadya na kumwa, ndipo ananyamuka noyenda. Esau anapepusa ukulu wake munjira iyi.