Mutu 4

1 Pamene Isiboseti, mwana mamuna wa Sauli anavela kuti Abneri afa ku Heberoni, manja yake yama foka, na bonse mu Isilayeli bana samba mutendele. 2 Manje mwana mwamuna wa Sauli anali na anyamata babili ana kuyanganila ma gulu ya ma silikali bankondo. Zina ya umozi anali Baana na wina Recabu, bana ba Rimoni M-beerotite, ochokela ku bantu bakuli Benjameni (Ndaba Beeroti azi dikiliwa bali ya Benjameni, 3 ndipo ma Beerotite anatabila ku Gittaimu ankala ili ku nkala kwamene kuja kuvikila ntawi ino) 4 Manje Jonatani, mwana wa Sauli, anali na mwana mwamuna anali chlema mu mendi yake. anali na zaka faivi pamene utenga wa Sauli na Jonatani kuchoka ku Jezreeli. kaboyi anayamuka ku tabanaye. Coma pamene anali kutaba, mwana wa Jonatani anagwa naku lemama. Zina yake enze Mefiboseti. 5 Pamene bana ba Rimmon mu Beerotite, Recabu na Baana, ana mutiwa yakupiya ija siku ku nyumba ya Isiboseti, pamene eza kupumula muzuba uja. 6 Muzimai olonda pa chiseko anagona tulo pamene enze kupepeta tiligu, na Recabu na Baana ana ngrna mwaka chetecete naku mupitilila enve. 7 Pambuyo o ngena manyumba, ana mugwaza na kumupaya enve pamene anali gone mu chipinda chake. ndipo ana mudula mutu naku yenda nawo, kunyenda munjila usiku onse kwa Arabiya. 8 Banaleta mutu wa Isiboseti kuli Davidi ku Heberoni, ndipo anakamba kuli mfumu, "Onani, uyu ndiye mutu wa Isiboseti mwana wa Sauli, mudani wako, wamene enze kufuna moyo wako. lelo Yehova aku bwezela bwana watu mfumu kuli Sauli na badwa mumbuyo." 9 Davidi ana yanka Recabu na Baana mubale wake, Bana ba Rimmoni mu Beerotite; anakamba kwa benve, "monga Yehova ankala, wamene ana moyo wanga mavutu yanga yonse, 10 pamene muntu wina anani uza, 'Onani, auli afa, 'kuganizila anali kunibwelesela utenga wa bwino, nino mugwila na kumupaya enve ku Zigilaki. ndiye malipilo nina mupasa na utenga wake. 11 Chili bwanji, pamene bantu boipa bakapiya muntu wakayele munyumba ili yake pogona pake, kondi sina zafusa magazi ku manja yake, na kumu choa pa ziko?" 12 Davidi analamulila kuli anyamata, ndipo bana ba paya naku badula manja na mendo naku ba pachika pamwmba pa bali mwa thanda ku Heberoni. koma bana tenga wa Isiboseti naku mu shika mu manda ya Abneri ku Heberoni.