Mutu 11

1 Inafika iyo ntawi yapa ntawi yamene ma mfumu yama yenda ku nkondo, pamene Davide anatuma Yowabu, wanchito wake, naba nkondo bonse bamu Isilayeli. Banaononga bankondo ba Amoni naku gonjesa Raba. Koma Davide ansala mu Yelusalemu. 2 Koma chinalikutu usiku umozi pamene Davide anauka kucjoka pogona pake naku yamba kuyenda pa malata ya nyumba yake ya chifumu. kuchoka kuja chinachitikila kuti anaona mukazi, ndipo mukazi wamene enze kusamba, ndipo mukazi anali wabwino kulingana. 3 Kuchoka apo Davide anatuma kufunsa bantu bamene banga zamu kazi uja. Winangu anakamba kuti, "nanga uyu si Batshiba, mwana mukazi wa Eliamu, elo nanga siwamene mukazi wa Uria mu Hititi?" 4 Davide anatuma ba tumwi bake naku mutenga; anabwela mukati kuli enve, ndipo iye anagona naye (pakuti anachokela chabe kuzilesa iye kuma matenda yoka magazi). Koma anabwelela ku nyumba kwake. 5 Mukazi anankala namimba, anatuma naku uzuza Davide, anakamaba kuti, "Nili namimba." 6 Ndipo Davide anatuma kwa Jowabu kukamba kuti, "Nitumizile Uria mu Hititi." 7 Pamene spo Yowabu anatuma Uria kuli Davide. Pamene Uria anafika, Davide anamufunsa kuti Yowabu alibwanji, namwamene nkondo inali kuyendela. 8 Davide anauza Uria kuti, "Yenda kunyumba kwako ukasuke mendo yako. "Pa ichi Uria anachoka kunyumba ya mfumu, ndipo mfumu anamutumizila Uria mpaso pambuyo pochokako. 9 Koma Uria anagona pakomo pa nyumba ya mfumu naba nchtio bonse ba mbuya wake, iye sanayende kunyumba yake. 10 Pamene bana mu uza Davide, "Uria sanyaende kunyumba kwake, "Davide anakamba kuli Uria kuti, "Nanga suna cjhoke paulendo? Nichani chamene sunyendele kunyumba yako?" 11 Uria anayanka avide kuti," Likasa, nama Isilayeli, nama Yuda bankala muma hema, na mbyua wanga Yowabu naba nchito ba mbuya wanga ba gona pa malo poseguka mu sanga, Manje ningayende bwanji munyumba mwanga kudya nakumwa naku gona namukazi wanga? ngati muli na moyo, sinizachita ichi." 13 Davide anauza Uria, "Nkala pani futi lelo, koma mailo niza kuleka kuti uyende. "Ndipo siku iyo na siku yokonkapo. 12 Pamene Davide anauitana iye, anadya nakumwa pamenso pake, Davide anapangisa kuti amwe maningi. Kumazulo Uria anayenda kugona pogona pake naba nchito ba mbuya bake; sanayende kunyumba yake iye. 14 Kuseni Davide analemba kalata kwa Yowabu, naku itumiza mumanja ya Uria. 15 Davide analemba mukalata kukamba kuti, "Mufake Uria kusogolo maningi kwamene kuli nkondo yolimba, ndipo mulekele enve, kuti amenyewe naku payiwa." 16 Ndipo pamene Yowabu enzekutamba kuzunguluka kwamu zinda anatumiza Uria pamalo pamene enzekuziba kuti bankondo adani babo bolimba bazayamba kumenyela. 17 Pamene bazimuna bamu muzinda banachoka naku menyana naba nkondo na Yowabu, benangu ba nkondo ba Davide bana gwesewa, ndipo Uria mu Hititi anapaiwa kuja. 18 Pamene Yowabu anatuma mau kuli Davide pali vonse vokuza nkondo, 20 analamulila ntumwi, kukamba kuti, ukasilisza ku uza mfumu pali vonse vokuza nkondo, 19 Chingachitike kuti amfumu banga kalipa, naku kamba kuli iwe, nichani chamene munayendela kufupi namuzinda kumenya nkondo? nanga simunazibe kuti banga ombele muchokela muchipupa? 21 Nindani wamene apaya Abimelelki mwana mwamuna wa Jerubi-Besheti? Nanaga simukazi wamene atema chintu kuchoka pamwamba pali enve kuchokela pachipupa kuti afele pa ku Tebezi? nichani chamene mwenze mwayendela maningi pafupi?' Ukayanke kuti, 'Wa nchito wanu Uria mu Hititi naye anafa.'" 22 Pamene apo ntumwi anachoka naku yenda kuli Davide naku mu uza vonse vamene Yowabu anamu uza vonse vamene Yowabu anamu tuma kuti akakambe. 23 Ndipo ntumwi anauza Davide, "badani banali na mpavu ku chila monga mwamene teuzelili payamba; banabwela kuli ise kunja kuja, koma tinabweza pakomo pongenela. 24 Pamene apo boponya babo bana ponya bankondo banu kuchokela mu vipupa, ba nchito bena ba mfumu na wa nchito wanu Uria mu Hititi anapayi wa naye." 25 Koma Davide anauza ntumwi kuti, "Ukambe ivi kuli Yowabu, 'Usalengesa kuti ivi, pakuti lupanga umameza umozi nafuti nawina nangu panga nkondo yako yolimba pa muzinda, naku gwesa, 'nakulimbiksa. 26 Pamene mukazi wa Uria ananvela kuti Uria mwamuna wake anafa kuti Uria mwamuna wake anafa, anadandula maningi pa bamuna bake. 27 Pamene kulila kwake kunsila Davide anatuma nakumupeleka kunymba yake ya ufumu, ndipo anankala mukazi wake naku kumubalila mwana mwamuna. Koma vamene Davide anachita sivinakondwelese Yehova.