Mutu 12

1 Pamene apo Yehova anatuma Nathani kuli Davide. Anabwela kuli enve naku kamba kuti,"Kunaliko bamuna babili mu muzinda. 2 Mwana umozi enzeli wolemela koma winangu ovutika. Mwamuna olemela anali nankosa na ng'ombe zambili maningi, 3 koma mwamuna vutika analibe kunja kwa ka mbalame ka ngono kakazi, kamene anagula naku pamozi naye nabana bake, Ka mbalame kanachokela mu chomwela chake, kanali kugoma mumnaja mwake ndipo kanali monga mwana mukazi kuli enve. 4 Siku imozi mulendo anabwela kuli mwamuna olemela, koma mwamuna senze ozipeleka kutenga ng'ombe kuti akonze chakudya cha mulendo. Mumalo mwake, anatenga ka nkosa kakazi kamwamuna ovutika naku kapikila balendo bake." 5 Davide anakalipa maningi pa mwamuna olemela, anauza Natani mwaukali, "Ngati Yehova niwamoyo, mwamuna wamene achita ichi afunika kumu paya. 6 Afunika kulipila nkosa kali folo futi chifukwa anachita chintu monga ichi, ndipo chifukwa sananvele chifundo pali mwamuna ovutika." 7 Apo Nathani anauza Davide kuti, "Ndiwe mwamuna! Yehova, Mulungu wa Isilayeli, akamba kuti, 'Ninakuzoza iwe mfumu pamwamba pa Isilayeli, ndipo ninakupulumusa kuchoka mumanja mwa Saulo. 8 Ninakupa nyumba ya mbuya wako, naba zikazi ba mbuya bako mumanja mwako. Ninakupasa futi nyumba ya Isilayeli na Yuda. Koma ngati vija vonse venzeli vingono, sembe ninakupasa vinangu vambili pambwa pake. 9 Chifukwa nichani wanyozela malamulo ya Yehova, pakuchita chamene nichoipa mumenso. mwake? unagwesa pansi Uria mu Hititi nalupanga naku tenga mukazi wake kukankala mukazi wako. Unamupaya na lupanga waba nkondo baku Amoni. 10 Chaicho lupanga suzaka choka munyumba yako, chifukwa waninyoza naku tenga mukazi wa Uria mu Hititi ngati mukazi wako.' 11 Yehova akamba kuti, 'Ona, nizaimya ngozi pali iwe kuchokela munyumba yako. Mumenso mwako, nizatenga bazikazi bako nakuba pasakuli bapafupi naiwe, ndipo bazagona nabazikazi bako muntawi yamu zuba. 12 Pakuti unachita uchimo wako mwizizizi, koma nizachita ichi chintu pamenso pa bonse ba Isilayeli, mu zuba. 13 Kuchokela apo Davide anauza Natani kuti, "Nachimwa kuli Yehova." Natani anayanka Davide kuti, "Yehova naye apita pali chimo yako. suzapaiwa. 14 KOma, chifukwa chachi chitdwe ichi wanyozela Yehova, mwana wamene aza badwa kuli mwana wa iwe zo-onadi azafa." 15 Pamene Natani anachokako naku yenda kunymba. Yehova anadwazika mwana wamene mukazi wa Uria anabala kuli Davide, enzeli odwala maningi. 16 Davide pamene apo ana pempela kuli Mulungu pa mwana mwamuna. 17 Davide anasala kudya naku yenda mukati naku gona pansi usiku onse. Bazikulu bamunyumba mwake bana nyamuka naku imilila pambali pali enve, kuti, bamushe kochokela pansi, koma sana imilile, sanadye nabo futi. 18 Chinafika kuti pasiku ya Sabata mwana anafa. Ba nchito ba Davide benze kunvela manta kumu uza kuti mwana wake afa. Pakuti bana kamba, "Onani, pamene mwana enzeli namoyo tinakamba naye, koma sananvelele mau yatu. Nichami chamene azazi chita tikamu uza kuti mwana wake afa?!" 19 Koma pamene Davide anaona kuti banchito bake bakambilana pamozi, Davide anaziba kuti mwana af. Anabauza banchito bake, "Nanga mwana afa?" Bana yanka kuti, "Afa." 20 Kuchoka apo Davide ananyamuka kuchoka pansi naku zisambika mwine wake, naku zizoza mwine wake, naku chinja vovalavake. Anayenda ku kachisi ya Yehova naku pembeza kuja. Ndipo kuchoka apo anabwela futi ku bantu bake. Pamene anachi pempa, banafaka vokudya pamenso pake, ndipo anadya. 21 Chokonkapo ba nchito bake banakamba kuli enve kuti, "Nanga nichani chamene mwachititla ichi? munasala kudya nakulililako pa mwama pamene anali na moyo, koma pamene mwana afa, mwanyamuka nakudya." 22 Davide anayanka kuti, pamene mwana anali na moyo ninasala kudy nakulila. Ninakamba kuti, 'Nindani wamene aziba kuti kapena iyayi Yehova azani komela mutima ine, kuti mwanna ankale na moyo? 23 Koma manje amwalila, nichani chamene nifunikila kusala kudya? Nanga mimga mubweza futi? Nizayenda kuli ine." 24 Davide anatotonza Batsheba mukzai wake, nakuyenda muli enve naku gona naye. Kupita kwa ntawi anabala mwana mwamuna, mwana bana mupasa zina Solomoni. Yehova anamukonda iye 25 naku tuma mau kupititla muli Natani muneneli kuti bamu teye zina ya Jedidia, chifukwa Yehova anamukonda iye. 26 Manje Yowabu anamenya na Rabo waku Amoniti, ndipo anatenga muzinda waku mafumu. 27 Pamene Yowabu anatuma ntumwi kuli Davide naku kamba kuti, "Namenyana Raba, ndiye natenga chopeleka manzi mu muzinda. 28 Chifukwa chake basonkaiza pamozi bonse bankonde bosalako naku mango pa zinda uyo naku utenga chifukwa nikutenga ine muzida, uzaitaniwa nazina yanga." 29 Pamene apo Davide anasonkaniza bonse bankondo nakuyenda kuli Raba; banamenya pamuzinda naku upoka. 30 Davide anatenga kolona kuchosa mumutu mwa mfumu-inalema ma talanta ya golide, munali namwala wamutengo mukati kolona inafakiwa pamutu pali Davide, kuchoka apo anachosa vofunuka vamu muzinda vambili. 31 Anchosa bantu bamene banali mu muzinda naku bapatikiza kuti basebenze na mpeni, mkwangwa za chisoluna nachisulo. anabangisa futi kuti basebenzese kwamene benze kupanga nchelwa. Davidi anafunsisa kuti muzinda zonse za bantu ba Ammoni bachite nchito iyi. kuchoka apo Davide na bankondo bonse bana bwelela ku Yesulamu.