MUTU 7

1 Pamemene Yesu anasiliza zonse zamene analikunena mukumvela kwabanthu, anangena mu kapenamu. 2 3 4 5 Koma musenchulion anali ndi kapolo wake wamene anakwezewa ngi iye, ndiponso analiodwala pafupi nakufuna kufa.Pamene musechulyoni anamvela paza Yesu, anatuma kwaiye akulu bama jews, nakumufunsa kuti abwele achilise wanchinto wake.Pamene banabwela kuli Yesu, Banamufunsa mosilizika, ndikunena, '' Nioyenela kuti iwe umuchitile izi, chifukwa akonda zikolatu, ndiponso niwamene anatimangila sinagogu yatu.'' 6 7 8 Pokapo Yesu anapitiliza munjila yake ndibemve.Koma pamene akalibe kufika patali nanyumba, Uja musenchulyoni anatuma banzake kuli iye, '' Ambuye, musazivutise, chifukwa inesindine oyenela kuti mubwele munyumba yanga. Kamba kachamene ichi sininazione kuti ndine oyenela kuti mubwele kwaine, Koma kamabani chabemau ndiponso wanchinto wanga azapola. chifukwa naine ndine munthu wamene alamulila asilikale. Nimane kuli uyu, 'kuti enda', ndiponso ayenda, ndiponso amanena kuli wina, ' bwela, 'ndiponso abwela, ndiponso kuli wanchito wanga, ' chita ichi, 'ndiponso amachita,'' 9 10 Pamene Yesu anamvela izi, Analiodabwisiwa ndi iye, ndiponso pakubwelela ku gulu lamene linali kumukonka, '' Ndikunena kuti, nikalibekupezapo chikululupilo monga ichi mu Izilaeli.'' Ndiponso banebenze naye banatumiwa kubwelela kunyumba, ndiponso banapeza kuti wanchito alibwino. 11 12 13 14 15 Kuchekela pamene apo Yesu anaenda kumuzinda wina oitanidwa Nani, Ndiopunzilabake ndiponso nagulu ikulu inaenda ndi iye. Pamene anafika pafupi ndikomo yamuzinda, Koma, mwamuna enzeokufa ananyamulidwa kuenda kunja, mwana mwamunaeka wamene bamaibake banali naye ( wamene anali ofedwwa), ndiponso gulu ikulu kuchoka mumuzinda banali ndi iye. Pamemene ambuye anamuona, Analiotengedwa ndichifundo paliemve ndiponso ananena kwaiye, '' kosalila.'' Ndiponso anapita kugwila mapulanga mwamene bananyamulila tupi, ndiponso bamene bana nyamula banaimilila.Ananena kwaiye, mwamuna wachichepele, ninena kwaiwe, nyamuka.'' Mwamuna wakufa anankala nakuyamba kukamba, ndiponso Yesu anamupasila kuli bamai bake. 16 17 Ndiponso bonse banagwilidwa ndi mantha, ndiponso banapitiliza kutamanda Mulungu, nakunena, '' Kuti muneneli mukulu anyamulidwa paliise'' ndiponso '' Mulungu ayanganila bana bake.'' Uyu utenga wabwino pali Yesu unasalangana konse mu Judeya ndiponso kulionse uzungulila zigao. 18 19 20 Aphunzila ba Yoani anamuuza palizonse izi.Ndiponso Yoani anaitana ophunzila bake babili ndikubatuma kwa ambuye ndikunena, '' Kodi ndimwe amene mufunika kubwela, olo tiyangani kuli winangu?'' Pamene bana bwela pafupi ndi Yesu, Azimuna ananena, '' Kuti Yoani mubadizi atituma kwaiwe ndikunena, ' Kuti kodi ndiwe wamene azabwela, olo tiyanganile winangu?'' 21 22 23 Paliija nthawi anachilisa banthu bambiri banalnda ndiponso analiomangidwa ndiponso kumizimu zonyansa, ndiponso kupasa menso kuosaona. Yesu anayankha ndikunena kwaiwo, '' pamene muzaenda munjila yanu, mukamu uze Yoani zamene mwaona ndiku mvela. bakungu bapenya, olemala alikuenda, bodwala kate batubisiwa, ovala matu bamvela, bakufa baukisiwa nakubwelela kumoyo, ndi aja opelebela auziwa utenga wabwino. Munthu wamene siasiya kukulupilila mwaine chifukwa chazinthu zamene nilikuchita niodalisika.'' 24 25 26 Kuchoka pamene batumiki ba Yoani bana enda, Yesu anayamba kunena pali Yoani, '' Nichani chamemene mwenzemwaendela panja muchipululu kuona? matete ananyan'ganisiwa ndi mpepo? Nanga wenze waenda panja kuona chani? Mwamuna omvala zovala