MUTU 5

1 2 3 Koma chinachitika kuti, pamene banthu bambiri analikuzingulila Yesu ndiponso kumvelela kumau ya Mulungu, analikuimilila pa nyanje ya Genazareti. Anaona maboti yabili yamene analikudonseledwa pamwamba ndikuya chosanakupeleka kumbali yamusinje. Baja bogwila nsomba ninshi bachokamo kudala ndiponso anali kusuka vogwililamo nsomba.Yesu anangena mu boti ina, yamene inali ya Simoni, ndiponso anamufunsa kuchosamo mumanzi pamalo yafupika muliyaja malo.Komanso anankhala pansi ndi kubauza bonse banali muboti. 4 5 6 7 Pamene anasiliza kukamba, Ananena kuli Simoni, '' Tenga boti ndiponso uipeleka pamanzi yamene yalimumalo mombila maningi pakuti mugwile.'' Simoni anayankha ndikunena kuti, ''Mfumu, tasebenza usiku onse, ndiponso sitinagwilepo kalikonse, koma kamba kamau yanu, nizangenesa zogwililamo nsomba pamanzi yombila.'' Pamene bana chita izi, bana unjika nsomba zambiri, ndiponso zogwililamo zao zinali kung'ambika.Koma banaenda kulibanzao bamene banali muboti inangu kuti babwele babatandizile.Banabwela ndiponso bana zuzha maboti yonse yabili, chakuti yanayamba nakumbila. 8 9 10 11 Simoni Petulo, pamene anaona ichi, anagwela pansi pamapazi ya Yesu, ndikunena, '' Chokani paliine, chifukwa ndine munthu ochimwa, Ambuye.'' Chifukwa chinamudabwisa, ndiponso ndi iwobameneanalinabo, pakugwila kwansomba zamene banatenga. Aba banali kuikilako Yakob ndiponso Yoani, mwana mwamuna wa Zebedi, bamenebanali kugwilizana nabopamozi ndi Simoni. Ndiponso Yesu ananena kuli Simoni, '' Usayope, chikukwa kuchokela manje uzayamba kugwila banthu.'' Pamene banaleta zongwililalo nsomba kunthaka, banasiya zonse ndikumukonka. 12 13 Chinabwela chachitika kuti pamene akali mumuzinda winangu, Munthu wamene anali ndi lepulosi analipo, Pamene anaona Yesu anagwesa manso yake ndi kumupempa, nakunena, ''Abuye, ngati mufuna, nitubiseni.'' Ndipo Yesu antambusula kwanja kwake ndi kumugwila, nakunena, ''Nifuna, nkhala otubisiwa.'' 14 Anamuuza kuti asauze aliyense, Koma anamuuza, '' Kuti enda njila yako, Ndiponso ukazilangize kuopeleka ansembe ndiponso upeleke chansembe pakutubisiwa kwako, kulinganiza mwane mose analamulila, monga umboni kwaiwo.'' 15 16 Koma mbiri paliiye anamwazikana patali, Ndiponso magulu yabanthu bambiri benzebanabwela kumvela vamene enze kupunzisa ndiponso anachilisa bambiri bamene benze bodwala.Koma anali kuchokapo nthawi yambiri nakubasiya noenda mumalo yobisika mukupempela. 17 Chinabwela chachitika chakuti, muyaja masiku yamene analikupunzisa, Ndiponso kunali afalisi ndi apunzisi amalamulo analichinkhalile kwamenekuja amene anabwela kumalo yambiri yaminzi zosiyana muzigao zija za muGalileyo ndiponso mu Judeya, ndiponso mumunzi wamu Jelusalemu.Mphamvu za Mulungu zochilisa zinali paliiye. 18 19 Koma bamuna bena bana bwela, ananyamula pampasa mwamuna wamene sianali kuyenda, Ndiponso anaona njila yomubweleselamo mukati pakuti amufake kuntangu na Yesu kuti amufakepo zanja.Sibana pezenjila yomupelekelamo mukati chifukwa kunali chigulu chabanthu, kamba kaichi banaenda pamwamba pa nyumba ndiponso banamuselusila pansi, pa mpasa yake, pakatika banthu, pantangu pamene analili Yesu. 20 21 Pakuona chikulupilo chao, Yesu ananena, '' Mwamuna, machimo yako yakululukidwa.'' Akalembela ndiponso Afalisi banayamba kufunsa izi, ndikunena, ''Kodi ni ndani uyu wamene akamba manyozo? Ni ndani angakululukile machimo koma Mulungu eka?'' 22 23 24 Koma Yesu, pakuziba zamene banali kuganiza, anayankha ndi kunena kwaiwo, '' Kodi nichani chamene mufunsila izi mumitima yanu? Nanga nichani chopepuka kunena, 'Kuti machimo yako yakululukidwa' loka kunena, 'Kuti ima uyende?' Koma kuti muzibe kuti mwana wa Munthu alina ulamulilo pazikolapansi kukululukila machimo, 'Ninena kwa iwe, 'Nyamuka uime, 'Tenga mpasa yako uyende ndiponso uyende kunyumba kwako.'' 25 26 Pamene apo anapita kuntangu kwao na kunyamula mpasa yamene analikugonapo. Ndiponso anabwelelamo kunyumba kwao, ndikutamanda Mulungu. Alionse anadabwa ndiponso banalemekeza Mulungu. Banazozedwa ndi kuyopa, nakunena, ''Kuti taona zinthu zamene zopambana lelo.'' 27 28 Pochoka kuchitika zinthu izi, Yesu anachoka mumalo yaja ndiponso anaona wamusonko zinalake ni Levi Analinkezi pajapa tenti pamene batengela musonko. Ananena kwaiye, '' Nikonke ine.'' Pomwepo Levi anaima ndiponso anamukonka, ndikusiya zonse pambuyo. 29 30 31 32 Koma Levi anapasa pwando ikulu kuli Yesu munyumba yake. Kunali bamisonko bambiri kujakumalo ndiponso banthu benangu banali kufendela kufupi na tebulo nakuyamba kudya ndi iye. Koma bafalisi ndiponso bakalembela banali kudandaula kubophunzila bake, nakunena, ''Kuti kodi nichani chamene udyela ndi kumwa nabamisonko ndiponso ndi ena ochimwa?'' Yesu anabayankha, ''Kuti banthu bamene sibanadwale sibangafune obachilisa, koma chabe bamene bodwala ndiye bangafune. Sininabwele kuitana bathu bolungama kulapila, koma kuitana ochimwa kulapila.'' 33 34 35 Ananena kwaiye, ''Kuti ophunzila ba Yoani bamakonda kupempela ndi kusala kudya kambiri, ndiponso ophunzila abafalisi bachitachimozimozi.Koma afalisi bako bakudya na kumwa.'' Yesu ananena kwaiwo, '' Kodi munthu angapange ukwati wa banthubake bamukwati nakubaleka kutibasale kudya, pamene mukwati akalinabo? Koma masiku yazabwela pamene mukwati azatengewa kwaiyo, Ndiponso masiku yaja bangasale kudya. 36 Koma Yesu ananena kwaiwo mukanthano. Kulibe anga ng'ambe chinyula muzigao kuchoka kuchanyowani ndiponso kusebenzesa kutungila kuchovala chakudala.Ngati anachita izi, Afunika ang'ambe chanyowani, Ndiponso chigao chanyula kuchoka kuchanyowani, sichinga fanile ndi chinyula chakudala. 37 38 39 Ndiponso kulibe angafake vinyu vanyowani mu vinyu vachikumba chakudala. Ngati angachite ivo, Ninshi vinyu vanyowani vinga pwanye chikumba. Koma vinyu vasopano vifunika kufaka muchikumba chanyowani. Ndiponso kulibe anamwa vinyu vakudala wamene angafune kumwa vanyowani, chifukwa anena, '' Kuti vakudala vilibwino.''