Mutu 48

1 Ina chitika pa mbofu paizi zintu, umozi anakamba kuli Yosefe, " Ona, atate bako ba dwala." Ndipo anatenga bana bake babili amuna , Manase na Efuraimu. 2 Pamene Yakobo ana uziwa, " Ona , mwana wako Yosefe afika kukuona," Israeli ana sakila mphamvu naku nkhala pa bedi. 3 Yakobo anti yosefe, " Mulungu wa mphamvu anaonekela kuli ine pamalo ya Luz mu Kanaani. Anani dalisa. 4 Ana kamba kuli ine, ' Onani, nizaku panga muntu ochuluka, naku kuchulukisa. Niza panga iwe muli maiko Yambili. Niza pasa malo aya kuli bo badwa mu mbuyo mwako na zintu zo yendelela. 5 Manje bana bako babili, anabadwa kuli iwe mu Egipito nikalibe ku bwela kuli iwe mu Egipito, ni banga. Efuraimu na Manase ni banga, monga mwamene Rubeni na Simeoni ni banga. 6 Bana bamene uza nkhale nabo kucho aba baza nkhala bako; baza nkhala bo pendewa ma zina pamozi nabo badiwa nabo potengo zo lobelela. 7 Koma pa ine, nika bwela ku choka ku paddani, kulila kwanga Rakele anafa mu malo ya kanaani mu njila, pamene panali mutunda kufika ku Epafra. Ninamu shika kuja pa njila yantu yaku Epafra" (Iyo ni Betelehemu). 8 Pamene Israeli anaina mwana wa Yosefe, anati, " niba ndani aba ?" 9 Yosefe anati kuli atate ake; " nibana banga, bamene Mulungu anani pasa kuno." Israel anati, " balete kuli ine, kuti ningaba dalise." 10 Tsopano menso ya Israeli yanali ku lepela chifukwa chau nkhalamba waka, ndipo sanali ku ona. Ndipo Yosefe anaba lefa pafupi nabo, anabafyofyonta nakuba kumbata. 11 Israeli anati kuli Yosefe, " Sininali oyemebekezale kuona pamenso panu futi, koma Mulungu ani vomekeza kuona bana bako." 12 Yosefe anaba chosa mukati ya mendo ya Israeli, analangana pansi mozichepesa. 13 Yose anaba tenga bonse babili, Efuraimu ku zanja la manja kufupi na kwanja ya mazele ya Israeli, na Manase ku kwanja ya mazele kufupi na kwanja ya manja ya Israeli, nakuba leta pafupi na eve. 14 Israeli anatambika zanja lake la manja naku ika pali Efuraimu pa muntu, wamene anali mufana, na kwanja ya mazele pa mutu wa Manase. Anapapambanisa manja yake, chifukwa Manase anali oyamba ku badwa. 15 Israeli anadalisa Yosefe, naku kamba ati, " Mulungu wamene atate banga Abrahamu na Isaki, Mulungu wamene anisunga kufika pano, 16 mungeli wamene anani cingiliza ku vofipi vonse, lekani aba anayamata aba. Lekani zina yanga itanidwe pali beve, na zina yaba tate banga Abrahamu na Isaki. Lekani bakule bochuluka pa ziko la pansi." 17 Pamene Yosefe anaona kuti atate bake bana ika zanja la manja pa mutu wa Efereimu sichinamu kondwelese. Ana tenga kwanja yaba tate bake nakuyi vendeza ku choka pa mutu wa Efureimu kuyi ika pa mutu wa Manase. 18 Yosefe anakamba kuli atate bake, " Simwamene, atate banga; uyu ndiye wachiyambi. Ikani zanja la manja pa mutu pake." 19 Atate bake bana kana no yanka, " Niziba, mwana wanga, niziba. Naye aza nkhala bantu, azankala opambana. Koma uyu mufana azankhala opambanapo kuchila eve, nabo badwa bake bazankala maiko yambili." 20 Israeli anabadalisa ija siku na mau aya. " Bantu ba Israeli baza kamba ma daliso pama zina yanu kuti, 'Ukani MUlungu akupanga monga Efureimu na Manase.'" Muli iyi njila, Israeli ana ika Efureimu pasongolo pa Manase. 21 Israeli anati kuli Yosefe, " Ona, nili pa fupi na kufa, koma Mulungu azankala naiwe, azaku bweza kumalo yaba tate bako. 22 Kuli iwe, monga muntu ali pamwamba paba bale bake, nakupaso chiguli chamene nina tenga kuli ma Amorites na lupanga na uta yanga."