Mutu 47

1 Ndipo Yosefe anangena ndipo anauza Farao, Atate banga na bale bannga, na nyama zabo na zosunga zabo ndi zonse zamene balinazo, bafika kuchokela kumalo ya Kanani. Ona, bali kumalo ya Gosheni." 2 Anatenga abale bake bamuna bali feivi ndipo anabazibisa kuli Farao. 3 Farao anakamba kwa abale bake, " Mugwila nchito bwanji?" Bana kamba kwa Farao, " Banchito banu ama onera mbelele, za makolo bantu." 4 Ndipo banakamba kuli Farao futi, " Ise tabwela monga alendo muno mumalo. Kulibe zodwesela nyama zabachito bananu, chifukwa kuli njala yopitilila mumalo ya Kenani. Sopano manje, napapata lolani banchito banu kukhale mumalo ya Gosheni." 5 Ndipo Farao anakamba kuli Yosefe, kukamba kutii, " Atate bako na babale bako babwela kuli iwe. 6 Malo ya Igipito yali pamaso yanu. Khazikisa ba tate bako ndi babale bako malo kudela ya bwino, malo ya Gosheni ngati uziba bamuna boyenera pakati pao, ubafake otsogolela zobeta." 7 Ndipo Yosefe analota Yakobo atate bake na baonesa kuli Farao. Yakobo anadalisa Farao. 8 Farao anauza Yakobo kuti, " Kodi wamkhala kwanthawi itali bwanji ?" 9 Yakobo anuza Farao, " zaka zakuyenda kwanga ni 130 zaka zamoyo wanga ni zing'ono ndipo zobaba. Sizambili ngati zamakolo banga banafa." 10 Ndipo Yakobo anadalisa Farao na kuchoka pameso yake. 11 Ndipo Yosefe anakhazikisa atate bake ndi abale bake. Anabapasa malo mudziko ya Igipito, malo opambana, mumdzinda wa Rameses, monga mwamene Farao anakambila. 12 Yosefe anapasa zakudya atatee bake, abale bake na onse bamunyumba mwabatate bake, kulingana ndi namba ya onse osungidwa. 13 Manje kunalibe zakudya mu ziko monse: cifukwa njala yenze yopilila. Ziko ya Igipito, na Kanani anaonongeka cifukwa ca mvula osankhalako. 14 Yosefe anaunjika ndalama zonse zinali mu Igipito namu Kanani, mogulisa zakidya kubantu. Ndipo Yosefe anapeleka ndalama ku malo ya amfumu Falao. 15 Pamene ndalama zonse za mu Igipito na Kanani zinasebenzewa, bantu bonse ba m Igipito banayenda kuli Yosefe kukamba kkuti, "tipase vokudya! Tizafela cni pamenso yako pakuti ndalama zathu zasila." 16 Yosefe anakamba kuti, "Ngati ngati ndalama zanu zasila, letani nyama zanu ndipo nizakupasani cakuddya mocinjana na nyama zanu. 17 Ndipo anabwelesa zosunga zao kuli Yosefe. Yosefe anabapasa cakudy mocinjana na mabulu, nyama siyana-siyana, zosunga zao na madonki. Anabadyesa mukate mocinjana na zosunga zao caka cija. 18 Pamene chaka china sila, bana bwela kwa ioe chaka chokokhapo ndipo bakamba kwa iye, " Siti zakubisani bwana kuti ndalama zonse zantu ndipo ngombe zonse ndi za bwana wanga kulibe zasalako mumaso bwana, kuchoselako matupi yatu napamene tikhala. 19 Nichifukwa chani tizafela pameso panu, ise pamozi na dziko yatu? Tiguleni, ndipo ise na dziko tizikhala banchito ba Farao. Tipaseni chakudya kuti tinkale namoyo kuti tisafe, na malo asankhala alibe kantu." 20 Ndipo Yosefe anagulila malo yonse ya Igipito Farao. Pakuti muntu aliyese wamu Igipito anagulisa munda wake, chifukwa kunali njala yopitilila. Munjila iyi, malo anakhala ya Farao. 21 Kuli bantu, banakhala akapolo bake kuchokela kumalile ena ya Igipito kufika kumalile kosiliza. 22 Nimalo aba sombe chabe yamene Yosefe sanagule, chifukwa basembe anabapasa zobatandizila. Banadya zobangabila kuchokela kwa Farao zamene anabapasa. Mwaiche sanagulise malo yao. 23 Ndipo Yosefe anakamba kubantu kuti, " Onani, nagulila Farao imwe na malo yanu lelo. manje izi ni mbeu zanu, zamene muzashanga mu malo. 24 Pa kukolola, mufinika kupasa Farao zachisanu ndipo mbali fo zizankhala zanu, chifukwa mbeu za mumunda ndi za chakudya niza munyumba mwanu nabana banu." 25 Bana kamba kuti, " Wapulumusa umoyo wantu. Tipeze chisomo mumenso yanu. Tizakhala ba chito ba Farao." 26 Ndipo Yosefe ana iyika lamulo yokokhewa mudziko la igipito kufikila lelo, kuti chachisanu chimozi ndi cha Farao. Malo chabe yabasembe niyamene Siyanakhale ya Farao. 27 Ndipo Israeli anakhala mu Igipito, mu malo ya Gosheni. Batu bake bankhala ndi zintau kumene kuja. Bana paka kwabili. 28 Yakobo anakala mu Igipito zaka seventini, ndipo zaka za umoyo wa Yakobo zinali handredi foti seveni. 29 Pamene nthawi yakufa kwa Israeli inafika pafupi, anaitana mwana wake Yosefe ndipo anati kuli yeve, " Manje napeza chisomo mwako, ika manja yako pansi pachibelo, ndipo unilagize kukulupilika ndi chilungamo. Napapata osanishika mu Igipito. 30 Nikagona ndi makolo achimuna banga, uninyamule kunichosa mu igipito naku nishika mu manda yamakolo banga bakudala." Yosefe anati, " Nizachita mwamene mwakambila." 31 Israeli anakamba, " Lapa kuli ine," Yosefe analapa kuli yeve. Ndipo Israeli ananguwesa mutu wake pongona pake.