Mutu 2

1 Ndipo kumwamba na ziko yapasi zinalengedwa, na onse vintu vamoyo, vamene vinazulamo. 2 Pa siku ya seveni mulungu anasiliza nchito zamene enzeli kuchita, ndiponso ana pumula pa siku ya seveni ku nchito yake yonse. 3 Mulungu anandalisa siku ya seveni na kuyi patula chifukwa musiku yakaena anapumula kuchoka ku nchito zake zonse zamene anachita mukulenga kwake. 4 Izi ndizochitika zokhudza kumwamba ndi dziko lapansi pamene zinalengedwa, pa tsiku limene Yehova Mulungu anapanga dziko lapansi ndi zakumwamba. 5 Panalibe chitsamba chamtchire padziko lapansi, ngakhale chomera chamthengo sichinamera, pakuti Yehova Mulungu anali asanavumbitsire mvula padziko lapansi, ndipo panalibe munthu wolima nthaka. 6 Koma kunkakwera nkhungu yotuluka pansi nathirira dziko lonse lapansi. 7 Yehova Mulungu anapanga munthu kuchokela ku doti yapansi, ndipo anamupemela mumpuno mpepo ya umoyo ndiponso munthu anankala wamoyo. 8 Yehova Mulungu anashanga munda ku maba mu Eden ndipo mwamene muja anaikamo munthu wamene anapanga. 9 Kuchokela kudoti yapansi yehova Mulungu analengasa mutengo uli onse ku kula zo oneka ku menso ndipo za bwino kudya. kufakilamo na mutengo na mutenga wa kuziwa chabwino na choipa. 10 Mumana unachikela mu Eden kutila munda. Kuchikela apo unamabikana ndipo unankala mimana zili 4. 11 Zina ya mumana oyamba ni Pishoni, ndiye yamene iyenda ku malo yonse ya Havilah, kwamene kuli golide. 12 Golide ya pa malo paja niya bwino. Pamalo paliko na bdellium na mwala wa onikisi. 13 Zina ya mumana wa chibili ni Gihoni. Weve uyenda mu malo yonse ya kushi. 14 Zina ya mumana wa chitatu ni Tigirisi, ndipo uyenda ku maba kwa Asuri mumana wa namba 4 ni Euferetesi. 15 Yehovah Mulungu unatenga mwamuna naku muika mu munda wa Edeni kuti azisebenzamo naku sungamo. 16 Yehova Mu analamulila mwamuna, kuti, " Ndiwe omasuka kudya kuli mutengo uli onse wa m'munda. 17 Koma kuchokela mu mutengo oziba vabwino na voipa osadya, chifukwa siku yamene uzakadyako, zoona zoona uzaka mwalila." 18 Ndipo Yehova Mulungu anakamba, "sichabwino kuti mwamuna ankale eka. Nizamupangila omutundiza omu wamila." 19 Kuchokela ku ooti, Yehova Mulungu anapanga nyama zonse zamuziko na nyoni zonse za mumwamba. Ndipo anavibwelesa kuli munthukuona vamene azaviyitana. chili chonse chamene munthu annaitana chilengedwe chai moyo chili chonse, yamene iyo yenze zina. 20 Munthu anapasa mazina ku vobeta vonse, ku nyoni zinse za mumwamba, ndipo naku nyama zonse zamu sanga. Koma kuli mwamuna eve kanalibe anapezeka omutandiza umilinga. 21 yehova Mulungu analengesa munthu kuti agone tulo tukulu ndipo mwamuna anagona. Yehova Mulungu anatenga mbambo imozi ya mwamuna naku valapo pa malo ya tupi pamene abatenga mbambo. 22 Na mbambo yamene Yehova Mulungu anatenga kuli mwamuna anapanga mukazi na kumubwelesa kuli mwamuna. 23 Mwamuna anakamba, "Manje apa, iyi ni bonzo yama bonzo yanga, na tupi ya tupi yanga. Azaitaniwwa mukazi chifukwa anachokela kuli mwamuna." 24 Chifukwa cha icho mwamuna aza choka panyumba ya batate bake naba mai bake no kubwela pamozi na mukazi wake ndipo babili aba baza panga tupi imozi. 25 Bonse babili mwamuna na mukazi wake banali chitako koma sibenzeli kunvela nsoni.