Mutu 19

1 Ba ngelo banabwela ku Sodom kumazulo, pamene Loti enzenkale pongenela mu muzinda wa Sodom. Pamene Loti anabawona, ananya mukka kuyenda kubatumanya , anangwada no paka mutu wake pansi. 2 Anakamba kuti, " Napapata bakulu banchito yanga, niku pempani kuti mubwele kuny' umba kwa wa chitowanu, munkale usiku, musambe naku meendo. Munganya muke kuseeni noyenda njila yanu." Bana yaanta, " Iyayi, tizagona pano pangila." 3 Anapapata cho koselela, banayenda na yeve nongena munyumba. Anakoza zokudya nopanga mukate ulibbe vopakisa, ndipo banadya. 4 pe bakalibe kogona, bamuna ba mumuzida, bamuna bamu Sodomu, bana zinguluka nyumba bana nabakulu bamuna boonse bamumizinda yonse. 5 Bana yitana Loti, banati kuli yeve, " balikuti bamuna bamene babwela kuli iwe usiku uno? balete kuli ise, tibazibe." 6 Ndipo Loti ananyenda panja pachiseko no vala chiseko kumbuyo kwake. 7 Akamba, " Namimpempani abbale banga, musachite zo chimwa. 8 wayonani, nilina bana bakazi babili bekakalibe kuziba mwamuna. nivomeleseni, niku papatani, kuti nibalete kuli imwe, ndipo muzachita zo kondwelesa aba, chifukwa bamu chinvili chamutenge wanga." 9 Banati, "bwelela mumbuyo! "Bana kamba nafuti, "uyu anabwela kunkala wachilendo, manje afina kunkala woweluza wata! Manje tizamuchita zoyipa kuchila beve." Banalimbana naye mwa muna, banalimbana na Loti, ndipo bana bwela pafupi kufuna kupwanya chiseko. 10 Ndipo bamuna banachosa kwanja no donsele Loti munyumba kuli beeve no vala chiseko. 11 Balendo ba Loti bna vela menso ya bamuna benze panja pa chiseko cha myumba, bana na ba kulu, ndipo banalema pe benzo josa kusakila chiseko. 12 Bamuna banakamba kuli Loti. "uliko nawuliwonse pano? Mupongozi mwamuna, mwna mwamuna, mukazi na uliwonse wako mumuzinda, bachose pano. 13 Tifuna kuwononga malo ano, chifukwa kulila kwawo kwavenka mamingi kuli yehova ndipo atituma kuti tiwononge malo ano." 14 Loti anayenda kukamba na azipongizi bake bamuna, bamuna bana lonjeza kukwala bana bake, anati, musanga, chokani pamalo aya, chifukwa Yehova afuna kuwononga muzinda."Kubapongozi bake bamuna chinawoneka monga a seka. 15 Pamene kunacha, angelo anawuza Loti, kuti, "yambani kuyenda, tenga mukazi wako na bana bako bakazi bali pano, musanyekele pamozi na chilango chamuzinda." 16 Anawayawaya. Ndipo bamuna bangwila kwanya kwake, kwanga kwamukazi wake, namanja yabana bake bakazi kuchoka mumuzinda. 17 Pebanabachoza panja, mwamuna umonzi anati, "Tamangilani umoyo wani! musayangene kumbuyo, usankale mumalo yalibe kantu kalikonse. Tamangila kulupili kuti musa nyeke." 18 Loti anati kuli Beeve, "iyaye, napapata, bakulu banchito yanga! 19 Wanchito wanu apeza chisomo pamenso yanu, anso mwanilangisa chifundo chopitilila mukupulumusa umoyo wanga. Ndipo siningtamangile kulupili, chifukwa chiwonongeko chachikulu chinganipeze, ndipo nizafa. 20 Wona, uja muzinda alipafupi maningi kutabilako, anso nikang'ono napapata, lekani niyenda (sikangono?), Ndipo umoyo wanga uzapulumuka. 21 Anamuwuzu iye, "Chabwino, Nivomekeza pempo iyo, siniza wononga muzinda ye wakamba. 22 Yendesa! tanamanga kja, sinizachita chilichose paka ufikeko." Ndipo uyu muzinda unali zowa. 23 Pamene zuba inekwele pa ziko Loti anali anafika ku Zowa. 24 Yehova analokesa nvula ya Saufa mu mulilo kuchokela kumwamba mu sodom na Gomora. 25 Ana wononga mizinda zija, an malo yalibe kantu kalikoonse , nazonse zamoyo zinanili mumuzinda, nazonse zomela pansi. 26 Ndipo mukazi wa Loti, anali kumbuyo kwake, anayangana kumbuyo, ana sanduka cuulu cha saulti. 27 Abrahamu ananyamuka kuseni, no yenda pa malo pamene enze anayimilila ana Yehova. 28 Anayanga pansi ku Sodoma na Gomora nowona, chusi chinyamuka kuchioka pansi monga chusi chamu fanasi. 29 Pomwe Mulungu ana wonnga muzinda wa maloyalibe chilichonse, Abrahamu anabwela mumaganizo ya Mulungu. Anatuma Loti kuchoka pakati pa chiwonengeko pamene anaeononga muzinda wamene Loti analikunkalamo. 30 Koma Loti anachoka mu Zowa kuyenda kunkala kupili nabana bake babili bakazi, chifukwa anali na manta kunkala mu Zowa. Anankhala mu cimubo ca mulipili. Eve na bana bake bakazi. 31 Mwana woyamba anawuza mufana wake, "batate bakakota, kulibe bamuna konse kulibe mwamuna azagona naise monga mweba machitila pa ziko la pansi. 32 Bwele, tiye timwese batate moba, ndipo tizagona nabo, kuti tusunge mbewu ya batate batu." 33 Uja usiku banapasa batate bawo moba. Ndiponso woyambila anayenda nongona nabatate bake; batate bake sibanazibe pe anagona, na pe anawuka. 34 Siku yokonkapo woyambila anawuka mung'ono, "nvela, nonangona nabatate usiku wapita, Tiye tibamwese moba lelo usiku nafuti, ndipo uzayenda kugona nabo, kuti tisunge mbwe yabatate batu." 35 Uja usiku nawo banapasa batate bawo moba, ndipo mung'ono anayenda kugona nabatate bawo. Batate bake sibanazibe pe anagona na pe anawuka. 36 Bana bonse babili ba Loti banankala na mimba yabatate bawo. 37 Woyambbila anabala mwamuna, ndipo anamupasa zina Mohabu. Anankala kolo wana Mobaiti balelo. 38 Ndipo mupana wake, anabala mwana mwamuna, no mupasa zina la Ben-ammi-nchipo anankala kolo wa mantu ba Ammoni ba lelo.