Mutu 17

1 Pamene Abramu anali ndi zaka naite naine, Yehohova anaonekela kuli Abramu ndipo anakamba, " Ndine Mulungu wamphavu zonse. Yenda pamanso panga, ndipo nshala ulibe chifukwa. 2 Ndipo ndizasimikiza mapangano yanga ndi ine, ndipo muzapaka nakupitilila." 3 Abramu anagwada moika wake pansi ndipo mulungu anakamba naye, nati, 4 " Kwaine, ona, chipangano changa chili naiwe. Unkhala tate wamaiko ambili. 5 Zina yako sizankhala Abramu, koma izakahala Abrahamu ndipo nakusankha unkhala tate wamaiko yambili. 6 Ndizakubalisa iwe zaona , ndipo nizapanga mitundu yambili kuchoka mwaiwe, ndipo mafumu azabadwa kuchokela kuli iwe. 7 Nizapanga chipangano pakati pa iwe na ine na obadiwe pambuyo iwe mumibado yao yonse kwa chipangano chamuyayaya, kukhala mulungu wako na obadwa kwa iwe pa mbuyo pako. 8 Nizakupasa iwe, na obadwa kwa iwe pa mbuyo pako, malo amene mukhalamo, malo yonse yamu canaan, malo yamene muzakhala nayo kwamuyayaya ndipo nizankhala mulungu wabo." 9 Ndipo Mulungu anati kuli Abrahamu, " Iwe, ufunika kusunga chipangano, iwe na obadwa kwaiwe pa mbuyo pako mumibado yao yonse. 10 Ichi ni chipangano changa, chamene iwe ufunika kusunga, pali ine na iwe na obadwa kwa iwe pa mbuyo pako: Amina bonse bafunika kudulidwa. 11 Bafunika kudulidwa khanda yakusogolo, na ichi chizankala chitsazo chachipangano changa pali ine na iwe. 12 Bana bonse bamuna bali namatsiku eyiti afunika kudulidwa, mumibado zabantu bako bonse. Kuikilapo na onse obadwa munyumba mwako na iwo amene aguliwa na ndulama kuli alendo amene si obadwa kwa iwe pa mbuyo pako. 13 Mwamuna amene abadwa munyumba mwako na wamene waguliwa na ndalama afunika kudulidwa. Mwaicho chipangano changa chizankhala mu nkhanda yanu mu chipangano chosasila. 14 Mwamuna aliyense wamene sanadulidwe na mu dulidwe wakanda yakusogolo afunika kuchotsedwa pakati pa bantu bake. Apwanya chipangano chonga." 15 Mulungu anakamba kuli Abrahamu kuti, " Mukazi wako Sara, osamuitana futi Sarai. Koma Sarah. 16 Nizamudalitsa, ndipo nizakupasa mwana mwamuna muli yeve. Nizamudalitsa, ndipo azankhala mai wamaiko ambiri. Mamfumu abantu azachokela kwa yeve." 17 Abrahamu anagwada nakuika mutu wake pansi, nakuseka ndipo anakamba mumtima wake, " Kodi mwana angabadwe kuli mwamuna alinazaka handiedi? Nizontheka bwanji Sarah, alinazaka naite, kubala mwana mwamuna?" 18 Abrahamu anakamba kuli Mulungu kuti, " Ishmaheli azankhalila pamaso panu!" 19 Mulungu anati, "Iyayi, koma mukazi wako Sarah azakubalira mwana wamwamuna, ndipo uzaka mupasa zina ya Isaki. Nizakhazikisa chipangano changa ndi iye chifukwa chipangano ndi chamuyayaya na obadwa pa mduyo pake. 20 Pali Ishmayeli, nakubvela. Ona, namu dalitsa iye ndipo nizamupanga kuchuluka kwambili. Azakhala tate wabana twove achimu amfumu ndipo azakhala dziko yaikulu. 21 Koma chipangano changa niza khazikisa ndi Isaki, wamene Sarah azakubalira iwe pa nthawi ino chaka chitubwera." 22 Pamene anasiliza kukamba nayo, Mulungu anachokapo pali Abrahamu. 23 Abrahamu anatenga Ishmayeli mwan wake mwamuna, na bamene bonse banabadwila mumfumba mwake, na bamene bonse banali munyumba mwa Abrahamu, ana dulidwa khanda yao ya kutsogolo pa tsiku yamene ija, monga mwamane mulungu anakambila naye. 24 Abrahamu anali ndi naite naine zaka zaku badwa pamene anadulidwa khada yaka yakutsongolo. 25 Ishmayeli mwana wake anali ndi zaka satini pamene anadulidwa khanda yake yakutsogolo. 26 Patsiku imene ija Abrahamu na Ishmayeli mwana wake mwamuna anadulidwa. 27 Amuna onse amumumba mwake anadulidwa naye, pamozi nabonse bana badwila munyumba na bonse bamene banagulidwa na ndalama tuchokele ku maiko yene.