Mutu 20

1 Kunachitika kuti kumalo yamene ayo yamozi kwenzeli mu ovuta wamene zina yake enzeli Shiba wamene mwamuna wa Bikiri, mu Benjamiti. Analiza lipenga naku kamba kuti, "Tilibe mbali muli Davide, kapena kunakala nachili chonse chloba muli mwana mwamuna wa Jesi. Lekani mwamuna aliyese ayende ku nyumba yake, Isilayeli." 2 Pamene apo bonse bazimuna bamu Isilayeli banamutaba Davide naku konka Shiba mwana mwamuna wa Bikiri. Koma Bazi muna baku Yuda banakonka mfumu yabo pafupi, kuchokela ku Yodani kufikila ku Yelusalemu. 3 Pamene Davide anabwela ku nyumba yake yachifumu mu Yelusalemu, anatenga bazikazi bakapolo bali teni bamene anabwela asiya kuti basunge nyumba yachifumu, naku bafaka munyumba nakubalonda anali kubapasa vonse vofunikila, koma senzeli kugona nabo futi bana valizi wa kufikila masiku yakufa kwao, kunkala monga banali bofelewa 4 Kuchoka apo mfumu inakamba kuli Amasai kuti, "Ifuna bazi muna bamu Yuda pamozi mumasiku yayatu; Ufunika kunkalapo pano, naiwe." 5 Pamene apo Amasai anayenda kutiana Yuda, Koma anachedwa kupitilila ntawi yamene ba mfumu bana mupasa iye. 6 Pamene apo Davide anakamba kuli Abishi, "manje Shiba mwana mwamuna wa Bikiri azati ononga maningi kupita namwamene Abisalomu anachita. Tenga banchita ba bwana wako, ba silikali banga nakumutangila iye, nangu bazapeza mizinda nakutiba. 7 Kuchoka apo bazi muna ba Yowabu bana mukonkamo mumbuyo, pamozi naba Keretiti naba Peletiti nabanonse bankondo bampavu. Bana siya Yelusalemu ku pilikishia Shiba mwana mwamuna wa Bikiri. 8 Pamene banali pachimwala chachi kulu chamene chiliku Gibiyoni, Amasai anabwela kukumana nabo. Yowabu enzeli vale chida chaba nkondo chamene anabwela avala, panali lamba mumusana mwake na ntuba mofakamo upanga. Pamene anayenda pasogolo, lupanga inagwa. 9 Pamene apo Yowabu anakamba kuli Amasai kuti, "nanga zili bwino naiwee, muswema wanga? Yowabu anatenga Amase mwkumugwila pandevu nakwanja yaku zanja lamanja kumu pyopyona iye. 10 Amasai sanaione fwaka yamene yenzeli kukwanja yaku mazela kwa Yowabu. Yowabu analasa Amasai mu malala ndiye matumbo yake yanatukila pansi. Yowabu sana mugwileko futi, Amasai anafa. 11 Kuchoka apo umozi waba zimuna ba Yowabu anaimila pali Amasai, naku kamba kuti, Ïye wamene avomelezana na Yowabu, nawamene ali wa Davide, akonke Yowabu. 12 Amasai anali kukunkuika muma gazi yake pakati pa njila pamene mwamuna anaona kuti bantu bonse bali imilile, ananyamula Amasai kuchoka munjila naku mufaka mumunda. Anamuponya nsalu pali iye chifukwa anaona bonse bana bwela kumuimilila. 13 Pamene bana muchosa munjila Amasai, Bonse bazimuna bana mukonkamo Yowabu, bonse bazimuna bana mukonkamo Yowabu mu pilikisha Shia mwana mwamuna wa Bikiri. 14 Shiba anapita mumutundu yonse ya Isilayeli ku Abel Beti Maaca, naku mazijo yonse ya Bikiriti bamene bana bwela pamozi naju pilikisha Shiba. 15 Bana mugwila naku mu gonjesa iye mu Abel Beti Maaca. Bana manga njila yaku zinga pa muzinda ku chipupa. Bonse bazimuna bamene benzeli na Yowabu bana chi menya chipupa kuti bachi gwese. 16 Chokonkapo muzi mai wanzelu analila mwakukuwa mumuzinda, "Nvela, nipema anvela, Yowabu! Bwela pafupi naine kuti nakambe naiwe." 17 Pamene apo Yowabu anabwela pafupi naye, ndiye muzimai anakamba kuti, "Nanga ndiwe Yowabu?" Anayanka, "Ndine." Chokonkapo anakamba kuli enve kuti, "Nvela kumau ya wanchito wako, "Ninvela." 18 Kuchoka apo anakamba kuti, "banali kukamba muntawi yaku olala kuti, 'Zo-onadi funa malangizo ku Abeli, 'na malangizo ayo yaza siliza nkani. 19 Tili muzinda wamene uli wa mutendele maningi nabo kulupilika mu Isilayeli. uyesa kuononga muzinda wamene ni mai mu Isilayeli. Nichani chamene ufuna kumelela cholowa cha Yehova?" 20 Pamene apo Yowabu anayanka naku kamba kuti, "Chinkale kutali, chinkale kutali naine, kuti nimele kapena kuononga. 21 Sicha zo-ona. Koma mwamuna wochokela kupili kuziko ya Efremu, otaniwa Shiba mwana mwamuna wa Bikiri, anyamula kwanja yake pa mfumu, Davide. Mupelekeni iye eke, ndipo niza nizamu chokamo kuchoka mu muzinda." Muzimai anakamba kuli Yowabu kuti, "Mutuu wake uzaponyewa kuli iwe pa chipupa." 22 Chokonkapo muzi mai anayeda kubantu bonse munzelu zake. Bana juba mutu wa Shiba mwana mwamuna wa Bikiri, naku uponya kuli Yowabu panja. Kuchoka apo analiza lipenga ndiye bazimuna bake bana chokamo mu muzinda, aliyense mwamuna kunyumba yake. Kuchoka apo Yowabu anabwelela ku Yelusalemu kuli mfumu. 23 Manje Yowabu enzeli pamwamba pali bonse bankondo bamu Isilayeli, ndipo Benaia, mwana mwamuna wa Yehoiadai anali pamwamba pali bonse ba Kereti napali bonse ba Peletiti. 24 Adoniramu enzeli pamwamba pali bazimuna bamene benze kuchitisa chitno zokakmiziwa, Jehoshafati mwana mwamuna wa AHiludi enzeli wolemba. 25 Shiva enzeli mulembi ndiye Zodaki na Abiata benzeli bansembe. 26 Irai mu Jairiti enzeli nduna ya mfumu.