Mutu 19

1 Yowabu anauziwa kuti, "Ona, amfumu balila naku dandaula pali Abisalomu." 2 kugonjesa ika siku kunasanduka kulila pa bonse bankondo, pakuti bankondo banachinvela kuti chinakambiwa ija siku, amfumu banadandaula pa mwana wabo mwamuna." 3 Basilikali banachokapo mwazi zizi kuyenda mumuzinda ya siku, mange bantu bamene bannvela manyazi bamatabila pamene bataba kuchoka kunkondo. 4 Amfumu banavala pamenso pao nakulila naliu yapamwamba, "Mwana wanga mwamuna Absalomu, Abisalomu, Mwana wanga mwamuna, mwana wanga mwamuna!" 5 Chokonkapo Yowabu anagena munyumba muli mfumu naaku kamba kuli enve kuti, "Mwanivesa chisoni nkpoe zaba silikali banu bonse lelo, bamene bapulumusaa umoyo wanu lelo, na umoyo wabana bamuna bany na wa bana bakazi banu, na myoyo zabazika bakapolo banu, 6 Chifukwa mukonda baja bamene bakuzondani, naku zonda baja bamene baki kondani. Lelo mwaonesa kuti asogoleli baba silikali naba silikali balibe mbali kuli imwe. Lelo nakululupila kuti ngati Abisalomu enze akali naumoyo, elo ise tonse tafa, icho sembe chaku kondwelesani. 7 Pa ichi manje nyamukani muyende panja naku kamba bwino kuli asilikali, pakuti nilumbila pali Yehobva, ngati simuzayenda, sipazankala kapena umozi mwamuna wamene azasala naiwe usiku uno. Ichi chizankala choipilako pali imwe kuchila ngozi zonse zamene zunakuchitikilaniponi imwe kuchokela pa unyamta wanu kufikila manje." 8 Pamene apo mfumu waimilila naku nkala pa get yamu muzinda ndiye banru bonse banauziwa kuti, "Onani, Amfumu bankala pa geti, "bantu bonse bana bwela pamenso pa mfumu. 9 Bantu bonse benze kushushana pabeka bamutundu yonse ya Isilayeli kukamba kuti, "Amfumu banati banati chosa ise kuchoka mumanja ya adani batu, nakuti pulumusa kuchoka mumanja mwaba Filistini, koma manje batabamo mu ziko chifukwa cha Abisalomu. 10 Abisalomu, wamene tinazoza pamwamba patu, afa ku nkondo. nanga nixhani chamene simukambapo vilivonse pazoleta amfumu?" 11 Mfumu Davide anatumiza kuli Zadoki nakuli Abiata wansembe kukamba kuti, "kamba nabazi sogoleli baku Yuda kukamba kuti, "nichani mwankala osilizila kuleta mfumu kuti ibwelele kunyumba ya chifumu popeza kukamba kwama Isilayeli kupasa mfumu mwai, kuti babwezewe kunyumba ya chifumu? 12 Ndimwe azibale banga, nyama yanga na fupa yanga. Nichani kansi chamene mwankalila bosilizila kubabweza amfumu?' 13 Kansi kamba na Amasai, 'Nanga sindiwe wanyama yanga nafupa yanga? mulungu chitani naine, maninigi futi, ngati sindwe mukulu wasitima waba nkondokuchokela manje apo pamalo ya Yowabu."' 14 Pamene apo anatengamitima yabazimuna bonse bamu YUda ngati mwamuna umozi. Banatuma kuli amfumu kukamba kuti, "Bwelela, iwe naba zimuna bako." 15 Pamene apo mfumu inabwelelpo naku bwela ku Yodani. Manje bazimuna baku Yuda banabwela ku Giligo kuyenda kukumana na mfumu nakuti bailete mfumu uko ko Yodani. 16 Shimi mwana mwamuna wa Gela, mu Benjamiti wamene enzeli waku Bahurimu, anayendesa naba zimuna baku Yuda kuyenda kukumana na mfumu Davide. 17 Kunali bazi muna wani sausande naenve bochokela ku Benjamini, na ziba wanchito wa Saulo, na bana bake bamuna bali fifitini naba nchito benzeli na enve bali twenti. 18 Bana oloka Yodani mu menso mwamfumu. Bana oloka pakuleta banja ya mfumu nakuchita vonse vamene baganizila kuti ichi nixha bwini shimiri mwana mwamuna wa Gelai anazi chepesa pamenso pa mfumu akalibe kuyamba ku oloka Yodani. 19 Shimi anakamba kuli mfumu kuti, "Osati, bwana wanga, kunipezaa uchimwa kapena kuitana poganizila voipa vamene wanchito wanu anachita, siku yamene bwana wanga mfumu anachoka mu Yelusalemu. Nipempa, mfumu asachifake kumutima. 20 Pakuti wanchito wanu aziba kuti analakwa. Onani, nichanifukwa chake nabwela lelo ngati oyambilila kuchokela muma banja yonse ya Yosefe kubwela kukumana na mwana wwanga mfumu." 21 Komo Abishiri mwana mwamuna wa Zeruia anayanka kuti,"Nanga Shimi apaiwa chifukwa kaichi, chifukwa anatembelela ozoza wa Yehova? 22 Chokonkapo Davide anakamba kuti, "Nichani chamene nia chita naiwe, iwe mwana mwamuna wa Zeruia, kuti lelo wankala mudani kuli ine? Nanga aliyense mwamuna una azapaiwa lelo mu Isilayeli? Popeza siniza kuti lelo ndine mfumu pali Isilayeli?" 23 Pamene apo mfumu anakamba kuli Shimiri kuti, "Suzafa." Mfumu inamu lonila iye nakulapa njazi. 24 Kuchoka apo Mefibosheti mwana mwamuna wa Saulo. anabwela kukumana na mfumu. Senze anavala kumendo yake, kapena kujubako ndevu zake, kapena kuchapa zovala kuchokela pasiku pamene mfumu wachokapo kufikila siku yamene zinabwela kunyumba mu mutendele. 25 Ndipo pamene anabwela kuchoka ku Yelusalemu kukakumana na mfumu, mfumu anakamba kuli enve kuti, "Nichani chamene sunayendelele naine, Mefibosheti?" 26 Anayanka, "Bwana wanga mfumu, wanchito wanga anani nama, popeza ninakamba kuti, ' nizakwela pabulu vovala kuti niyende namfumu, chifukwa wanchito wanu niolemala. 27 Wanchito wanga ziba ananiama ine, wanchito wanu, ku bwana wanga mfumu. Koma bwana wanga mfumu alimonga mungeli wa Mulungu. Chaicho, chitani chamene chili cha bwino mumenso yanu. 28 Pakuti bonse bamunyumba mawa atate banga banali azimuna bakufa pamenso pa bwana wanga mfumu, koma munaika wanchito wanu pali abo bamene banadyela pa tebulo yanu. Nimpavu bwanji paichi zamene nili nazo kuti nipilize kulila kuli mfumu? 29 Kuchoka apo mfumu wakamba kuli enve kuti, "Nichani upiliza ku londolola? Naganiza kuti iwe na ziba mu gabne minda." 30 Pamene apo Mefibosheti anayatuka mfumu kuti, "inde, lekani atenge onse, popoza bwana wanga mfumu abwela kunymba yake mwamutendele." 31 Chokonkapo bazilai mu Giliditi anabwela kuchokela ku Rogilimu kuoloka Yodani na mfumu nakupelekeza mfumu pamwamba pa Yodani. 32 Manje Bazilai anali mwamuna nkalamba, na zaka zili 8. Anakonzekela mfumu navakudya pamene enze kunkala ku Mahanaimu, pakuti enzeli mwamuna wolemela. 33 Mfumu anakamba kul Bazilai, " 34 Bazilai anayanka amfumu kuti, "Nimasiku yangati yamene yasalako muzaka zaumoyo wanga, kuti niyende namfumu mu Yelusalemu? 35 Nilina zaka 80. Ninga siyanise pali chabwino na choipa nanga? nanga wanchito wako angalabe vamene nimadya kapena vamene nimamwa? Ninga nvele futi boumba nanga? nichani chamene wanchtio wako okuvulisa kuli bwana wako mfumu? 36 Wanchito wako azafuna kuti chabe ayendeko pamwamba pa Yodani na mfumu. Nichani chamene mfumu azanilapila nampoto ya so? 37 Nipempa kuti lekani wanchito wanu abwelele kunyumba, kuti nikafele mumuzinda wanga pa manda ya tate naba mai banga. koma onani, uyo wanchito wanu Kimhamu. Lekani kuti awoloke na bwana wanga mfumu, naku chitila iw=ye chamene chioneka chabwino kuli imwe." 38 Amfumu bana yanka kuti, "Kimhamu azayenda naine, ndipo nizamuchitila iwe, nachili chnse chamene ufunisisa kuchokela kuli ine, nizakuchitila ine." 39 Kuchoka apo bantu bonse bana oloka Yodani, naba mfumu bana oloka, mfumu anapyopyosa Bazilali nakumu dalisa iye. Choknkapo Bazilai anabwelela kunyumba yake. 40 Pamene apo mfumu aaolokela ku Giligo, Kimhamu naye anawoloka naye. Bankondo nonse baku Yuda banaleta mfumu, nabenangu bankondo bamu Isilayeli. 41 Mwamusanga azimua bamu Isilayeli banayamba kubwela kulimfumu naku kamba kuli mfumu kuti, "CHifukwa nichani azibale batu, ba zimuna bamu Yuda, banakubani naku kubweza mfumu na baja yake pa Yodani, na bonse bazimuna ba Davide naimwe?" 42 Pamene apo bazimuna bamu Yuda banayanka bamuna bamu Isilayeli kuti, "nichifukwa chakuti mfumu nimubululu watu wapafupi. Pali ichi? Nanga tadya chilichonse chamene mfumu ifunikila kulipila? Batipasako panso iliyonse?" 43 Chokonkapo bazimuna bamu Isilayeli banayanka bazimuna baku Yda kuti, "Tili namitundu yokwanilamo teni yachibululu kuli mfumu, ndiye tilina ulamulilo wambili pali Davide kuchila imwe. Nanga nichani munati zondela ise? Nanga sikuvomeleza kwatu kuna yambililila kunveka kuti mfumu yatu ibwelele? Koma mau yabazi muna baku Yuda yanankala yaukali kuchila mau yaba zimuna bamu Isilayeli.