Mutu 1

1 Pambuyo ya infa ya Saulo, Davide anabwelako muku menyana nama Amalakati na kusalila mu zigilaki kwa masiku yabili. 2 Pasiku ya chitatu, mwamuna anachoka ku campu ya Saulo na zovala zongambika na doti mu mutu. Pamene ana bwale kuli Davide anagwa pasni naku gwada pansi. 3 Davide ana kamba kuli enve, "wachokela kuti? "ana yanka, "na taba ku campu ya Isilayeli, " 4 Davide ana kamba kuli enve, "Zo'ona niuze mwamene vintu vayendela. "ana yanka, "Bantu bataba ku nkondo. babili bagwiliwa na babili banafa. Saulo na Jonathani mwana mwauna na enve afa." 5 Davide anakamba kuli munyamata wachi chepele, " waziba bwanji kuti Saulo na Jonathani mwana wake kuti bafa?" 6 Munyamata wachichepele anayanka, "Mwamwami ninali pa piri ya Giliboa, ndipo paja Sauloo anashintilia pali mukondo wake, na ngolo na oyendesa akavalo benze pafupi kumugwila enve. 7 Saulo ana pindimuka nakuni ona ine ndipo anani itana inw, 'nina yanka,' nili pano. 8 Ana kamaba kuli ine, 'Ndiwe ndani iwe?" nina muyanka enve, 'ndine mu Amaleki.' 9 Anakamaba kuli ine, 'Napapata imilila oali ine ndipo unipaye ine, mavuto yani gwila maningi ine, koma nikali na moyo waine.' 10 Chakuti nina imilila kuli envw na kumupaya, chifukwa nna ziba kuti saza nkala moyo pambuyo ya kugwa. ndipo na tengo korona yamene inali pa mutu pake na bandi yamene inali pa kwanja yake, nakuvileta kuli imwe, abwana banga." 11 Pamene apo Davide ana ng'amba vovala vake, na bantu bonse banali naenve bana chita chimozi mozi. 12 Pamene apo banalila, kuchosa misozi, na kusala kudia kufikila mumazulo kwa Saulo, na Jonathani mwana wake mwamuna, ku bantu ba Yehova,na nyumba ya Isilayeli chifukwa ba nagwa kupanga. 13 Davide anakamba kuli munyamata wachichepele, "uchokela kuti?" ana yanka, "ndine mwana mwamuna wamulendo mu malo, mu Amaleki." 14 Davide anakamba kuli enve, "Chifukwa chani sunayope kupaya Yehova ozozewa fumu na kwanja yako?" 15 Davide ana itana umozi munyamata wachichepele na kukamba kuti, "yenda kamupaye enve." Chakuti munyamata ana yeda naku mupaya, ndipo mu Amaleki anafa. 16 Davide anakamaba kuli wakufa mu Amaleki, "magazi yako yali pa mutu pako chifukwa kamwa kako kachitlia umobi kuku ukila iwe naku kamba kuti, napaya Yehova ozozedwa fumu.''' 17 Davide ana imba nyimbo kwa Saulo na Jothani mwana wake mwamuna. 18 Analamulila bantu ku punzisa iye nyimbo ya uta bana ba Yuda, yamene ina lembewa mu buku ya Jashar. 19 "Uleme wanu, Isilayeli, unapaiwa pamu sanje yako. Ha! anagwa wampamvu! 20 Mu sazi uze kwa Gati, usa chikamba ichi mumiseu ya Asikeloni, kuti bana ba kazi a Filisti anga sekere, kuti bana bakazi a osaduliwa asa kodwere. 21 Lupili ya Gilibowa, kusankale mame mwania vula pa iwe, mwina mumunda kupasa chakudya cha ulele, kwaicho chi shango cha ????? zonse china desewa. Chishango cha Saulo sicho zozwewa na futi na mafuta. Kuma Gazi yabo bamene bana paiwa, kuma tumpi ya ???? zonse china desewa. Chi shango cha Saulo sicho zozewa na futi mafuta. 22 Kuchokela kumagazi yabo bamene ban paiwa, kuma tumpi ????, uta wa Jonathani sunabwelela ndipo lupanga wa Sauli una bwelel chabe. 23 Saulo na Jonathani benze bo kondwelesa ndi okoma muyo zabo, ndipo namu infa yabo sibana patuliwe. anali nayo liwiro yopabana chiombankanga, benze bolimba ku pabana mukango. 24 Imwe bana bakazi bamu Isilayeli, mulileni Saulo, wamene ana valikani imwe zofira zokometststa, wamene anaika vokometsetsa va golide pa vovala vanu. 25 Monga ba phamvu anagwa pakati pa ankondo! Jonathani apaiwa pamu sanje pako. 26 Ndipo sinjika mutima chifukwa chaiwe mbale wanga Jonathani. Weze oni komela kwambili. chikondi chako kwa ine china chodabwisa, kupitilila chikondi cha mukazi. 27 Monga ba mpamvu anagwa, na zida za nkondo zina onongeka!"