Mutu 23

1 Chakuti mfumu anatuma bopeleka utenga bana sonkanisila bakulu ba Yuda na Jerulasalema. 2 Pamene apo mfumu anayenda ku nyumba ya Yehova, naba muna bonse ba Yuda na bonse be bankala mu Jerusalema na enve, na bakulu bang'ono kufikila kuba kulu. Anababelengela mau ya buku yachipangano inapezeka munyumba ya Yehova. 3 Mfumu inaimilira mu comangiwa citali nakupanga cipangano na Yahwe, ktui aayenda na Yahwe na kusunga malomulo, nakukonkha okamba na zolembewa zake na mtima wanthu wonse na moyo wanthu wonse ku vomelea mau ake acipangano zolembewa mubuku. Banthu bonse kusunga cipangano. 4 Mfumu analamulira wansembe Hilkiah, wansembe wake, na oimilila pa colobela kuti abwelese vonse vopangiwa na Baal na Asherah, na nyenyei zonse zakumwamba. Ana shoka zonse panja pa Yerusalemu mu munda mu Kirdron vali ndipo banatenga milota yao ku Bethel. 5 Anacosa milungu yonse yopangiwa na ansembe amene mfumu ya Yuda anasankha ku shoka zonunkhila pamwamba pa malo ya Yuda mu malo ya Yerusalemu - baja bana shoka zonunkhila kwa Baal, ku zuba na mwezi, mumwamba na ku nyenyezi zonse. 6 Anacosa cifanizo copangiwa mu tempele ya Yahwe, kunja kwa Yerusalemu ku Kidron vali ndipo banachishoka kuja. Anaononga ku igaya kunkhala dothi nakuziika ku manda ya banthu ba pansi. 7 Anakonza monkhala muja mwa mahule aja bamene benzeli mu nyumba ya Yahwe, kwamene akazi anapanga nyula zosintha ku cifanizo. 8 Josiya anachosa ansembe onse mumuzinda wa Yuda naku yipisa malo yapa mwamba pamene wansembe anali kushokela zofukiza, kuchokla ku Geba kufikila ku Beresheba. Anawonga malo yapa mwamaba pa chipata chinali pongenela chipata cha Yoshuwa (kazembe wamu muzinda), kumazere kwa chipata cha muzinda. 9 Ngakale wansembe wa malo yapamwamba yoja sebenze bovomelesewa kutumikila pa guea ya Yehova mu Jerusalema, banadya muate unalibe vofufumisa bakati pa abale babo. 10 Josiah anaononga Topheth, yamene ili mu malo ya Ben Hinnom, kuti pasapeeke wopangisa mwana mwamuna kapena mukazi, kupita pa muliro ngati nsembe ya Molech. 11 Anacosa akavalo yamene mfumu ya Yuda inapeleka ku uba. Banali pa malo yenango pafupi na pongenela pa tempele ya Yahwe, pafupi na Nathan - Melek, mdindo . Josiah anashoka ma kavalo yopelekewa ku zuba na muliro. 12 Josiya mfumu anawononga ma guwa anali pa mutengo wapa chipinda chapa mwamba cha Ahazi, yamene mfumu ya Yuda anapanga, nama guwa yamene manese enze anapanga mu makoti yabili yamu tempele ya Yehova. Josiya anazipwanya muzi dunswa nakuzitaya mu chigawa cha kidroni. 13 Mfumu anawononga malo yapa mwamba kumawa kwa Jerusalema, kumazulo kwa lupili lazipupu zamene Solomoni mfumu wa Isilayeli wa anamangila Ashtoreth mafano yonyansa yobaku Sidoni; ya chemoshi, mfano yonyansa ya Moabu; naya Moleki, mfano yonyansa ya bantu ba Amoni. 14 Anatwola mapilala ya myala muzi dunswa dunswa naku juba mitengo ya Ashira nakuzuzya malo yaja nama fupa ya bantu. 15 Josiya anasiliza kuwononga ma guwa anali ku Bethel napa malo yapa mwamba yamene Jerobomu mwana wa Nebat wamene analengegesa Isilayeli ku chimwa anamanga. Ana shoka guwa na malo yapa mwamba nakuyimenya paka kulukungu. Anashoka mutengo wa Ashira. 16 Pamene Josiya anayanganila malo, anawona manda anali kumbali kwa lupili. anatuma bamuna kuti batenge mafupa kuchokela mu manda; ndipo anavishoka pa guwa, ina yipisa. Uku kunali kukonnkeleza mau ya Yehova yamene muntuu wa Mulungu anakamba, mwamuna wamene anakamba vintu ivi vikali kuchitika. 17 Ndipo anakamba, " Coumbiwa cabwanji ichi niona?" Amuna amu muzinda anamuza. " Aya ni manda ya munthu wa Mulungu amene anacokela ku Yuda ndipo anakamba pa vinthu vamene mwacita pa guwa ya Bethel." 18 Ndipo Josiah anakamba, " Ilekeni yeka. Pasapezeke wotenga mafupa." Muyaleke yeka mafupa ya mneneri amene anacoka ku Samaria. 19 Pamene apo Josiya anachosa manyumba yonse pa malo yapa mwamba yanali mumizinda ya Samaria, yamene mfumu ya Isilayeli anapanga, analengesa Yehova ku kalipa. Anachita kuli benve vamene zinachitiwa ku Bethelo. 20 Anapaya bansembe bonse bapamalo yapamwamba pa guwa ndipo anasjokela yabantu pali zenve. Anabwelela ku Jerusalema. 21 Mfumu inalamulira banthu bonse, kuti, " Mucitere Yaweh Mulungu wanu pasika, monga nicolembewa mu buku ya cipangano." 22 Pasiku yaso sinacitikepo kucoka pa nthawi ya owerua ba Israyeli, kapena mu masiku ya mafumu ya Israyeli kapena Yuda. 23 Koma mu caka ca eitini ca mfumu Josiah pasaka ya Yahwe ina sangalira mu Yerusalemu. 24 Josiya anapilikisa baja banaliku kamba nabo kufa olo namizimu. Anapilikisa futi naba umfwiti, mafano, nazintu zonse zonyase zenzo oneka mu ziko ya Yuda namu Jerusalema, chakuti basimikizike mau ya lamulalo yanali yolembewa anapeza munyumba ya Yehova. 25 Kumbuyo kwa Josiya, kunalibe mfumu monga enve, anayangana kuli Yehova namutima wake onse, ,oyo wake onse, na mpavu zake zonse, anakonkeleza malamulo yonse ya Mose. Ndipo panalibe mfumu yina monga Josiya inayima pambuyo pake. 26 Koma, Yehova sanachinje kukalipa kwake koyofya, kwe anakalipila Yuda chifukwa cha vonse Manase anachita kulengesa kuti akalipe. 27 Yehova anakamba kuti, "Niza chosa futi na Yuda pamenso panga, mwenachosela Isialyeli, ndipo nizatenga uyu muzinda wenasanka, Jerusalema, na nyumba yamene ninakamba kuti, zina langa lizankalapo." 28 Koma kukamba zankhani zina zokamba pa Josiah, zonse anacita, sizinalembewe mu buku yazocitika za mfumu ya Yuda? 29 Mu masiku aja, Farao Necho, mfumu ya Egypto, anayenda kumenyana na mfumu ya Assyria ku kamana ka Euphrates. Mfumu Josiah anayenda ku kumana na Necho mu nkhondo, na Necho anamupaya pa Megiddo. 30 Wanchito wa Josiah anamutenga pa gareta kucosa pa Magiddo, ku muleta ku Yerusalemu, anamuika mumanda yaje. Ndipo banthu ba mu malo anatenga mwana wake Jehoahaz mwana mwamuna wa Josiah, nakumuzoza eve, kupanga ankhale mfumu mu malo mwa atate bake. 31 Jehoahaz anali wa zaka twenti - fili pamene anayamba ku lamumulira, analamulira miyezi fili cabe mu Yerusalemu. Amai bake bake zina yabo yezeli Hamutal; banali mwana mukazi wa Jeremiah waku Lubinah. 32 Jehoahaz anacita coipa ku mnso kwa Yahwe monga makolo bake bonse banacitila. Farao Necho anamuika mu macheni ku Riblah mu malo ya Hamath, Kuti nasalamulile mu Yerusalemu. 33 Ndipo Necho anamupasa mtenga Yuda makhumi khumi yama talente yasilira talente imozi ya golide. 34 Farao Necho anapanga mwana mwamuna wa Josiah Eliakim mfumu mumalo mwa atate bake Josiah, anachinja zina yake kunkhala Jehoiakim. Koma anatenga Jehoahaz kucoka ku Egypto, na Jehoahaz anafela kuja. 35 Jehoiakim analipila siliva na golide kuli Farao. Ndipo kwanilisa kufuna kwa Farao, Jehoikim kusonkhesa malo kubakakamiza pa anthu , mumalo aba kuti apeleke kwaiye siliva na golide monga mwa kufuna kwake. 36 Jehoiakim anali nazaka twenti-faive pamene anayamba klamulila, analamulila kwa zaka ileveni mu Jerusalema. Zina yaba mai bake inali Zebida; anali mwana wa Pedaia waku Rumah. 37 Jehoiakim anachita zochimwa pa menso ya Yehova, monga zonse makolo bake banachita.