Mutu 22
1
Josiah anali nazaka eiti pamene anayamba kulamulira, analamulira zaka feti-wanu mu Yerusalemu. Zina ya bamai bake yeze Jedidah ( mwana mukazi wa Adaiah waku Bozkath).
2
Anacita camene cizeli coyenera pamenso pa Yahwe. Atate bake Davidi banayenda, sana chinje kapena kuyenda ku liiti olo ku lefuti.
3
Inafika mu mwaka wa eyitini ya Josiya mfumu. anatuma Shapani mwana wa Azaliya mwana wa Meshullamu, mutembi, munyumba ya Yehova, Kuti,
4
"Yenda kuli Hilkiah mukulu wansembe umu'uze kuti apende ndalama zamene zaletewa kachisi bana tenga kubantu.
5
Zipasiwe mumanja ya ogwira nchito bebayangana nyumba ya Yehova, ndipo bapase bogwila nchito bali mu nyumba ya Yehova, kti bapange zowonogeka mu tempele.
6
Balekeni bapase ndalama kuli opala mapulanga, naomanga, naogula mapulanga ndipo bajube miala bakone tempele."
7
Koma kunalibe kubelenga ndalama zamene anapasiwa, cifukwa anazisunga mokhulupilika.
8
Hilkiah wa nsembe mkulu anakamba kuli Staphan olemba, " Napeza buku ya malamulo mu nyumba ya Yahwe." Ndipo Hilkiah anapasa buku Staphan, ana ibelenga.
9
Staphan anayenda nakutenga buku kupasa mfumu, anapeleka ripoti kuli eve kukamba, " Banchito basebenesa ndalama zamene banapeza mu tempele naku pasa bosebenza mu tempele nbamene basunga nyumba ya Yahwe."
10
Pameno apo Staphan olemba anakamba kuli mfumu, " Hilkiah wa nsembe mkulu anipasa buku." Ndpipo Staphan anaibelenga.
11
Zinali pamene mfumu anamvela mau ya malamulo, anang'amba vobvala vake.
12
Mfumu inalamulira Hilkiah wa nsembe, Ahikam mwana mwamuna wa Staphan, Akbor mwana mwamuna wa Micaiah, Staphan olemba , na Asaiah, wanchito wake, kukamba,
13
" Yenda ndipo ufunsekuli Yahwe pamalo paine, na bonse banthu na yonse Yuda, cifukwaca mau yamene napeza mubuku iyi. Ukali wake niuukulu Yahwe wamene wayakila ife cifukwa ca makolo batu sibanamvele vamene buku iyi ikamba kuti bakonke vonse vamene vinalembewa pali ise.
14
Ndipo Hilkiah wa nsembe, Ahikam, Akbor, Staphan, na Asaiah banayenda kuli Huldah muneneli, mukazi wa Shallum mwana mwamuna wa Tikvah mwana mwamuna wa Harhas, osunga maika vovala ( anankala mu Yerusalemu mu kota yanamba tuu), na kukamba naye.
15
Anabauza beve, " Ivi ndiye vamene Yahwe, Mulungu wa Israyeli, akamba: ' Muuze mwamuna akutumani kuli ine,
16
Ivi ndiye vamene Yahwe akamba: ' Ona, Niza bwelesa coipa mumalo yano na vonse vonkhalamo, kulingana na vamene vina lembewa mubuku yamene mfumu ya Yuda yabelenga.
17
Chifukwa mwanisiya nakushokela vonunkila kuti milungu twenangu , chakuti banilengesa kukwiya namachitidwe yeba chita-Koma lu kwiya kwanga kwayasa pamalo aya, ndipo sikuza zimiwa."'
18
Koma kuli mfumu ya Yuda, anamitumani kufunsa Chifunilo cha Yehova, Ivi ndiye ve muzayena kumuwuza: "Yehova, Mulungu wa Isilayeli akamba kuti: konkaniza na mau ye ananvela,
19
chifukwa mutima wako unali wofewa, ndipo chifukwa unazichepesa kuli Yehova , pamene unanvela venina kamba pali aya malo na bonse bebankala mo, kuti bazakankala bwinja na tembelelelo, ndipo kuli ine, naine niminvelani-uku ndiye kulengesa kwa Yehova.
20
Ona, niakuika pamozi na makolo yako, ndipo uaikiwa mumanda mwako mu mtendere. Menso yako siyazaona zonse zoipa zamene nizaika pali malo yano.""" Ndipo bamuna banapeleka uthenga kuli mfumu.