MUTU 1

1 2 3 4 Bambili banaesa kufaka mundanda nakufotokoza pazinthu zamene zinafikiliziwa kwaise, monga mwamene anazipasila kwaise, bamene pachiyambi banayanganila umboni na menso ndi atumiki bautenga.Ndiponso kwaine chinaoneka chabwino_pakuona kuti anafunisisa bwino kamba utenga wazinthu zonse kuchoka pachiyambi_ polemba mundandanda pazaiwe, Ichi nichabwino theofilas.Ichi chinali mwatelo pakuti uzi chonadi pazinthu zamene zinakambiwa. 5 6 7 Mukusilizila kwamisiku ya Herodi, mfumu ya mujudeya, kunanali winawache opeleka wansembe oitanidwa zina Zakaliya, kuchokela kuchigao cha Abiyah.mukaziwake anachokela pabana bakazi ba Aaron,ndi zina yache inali Elizabeta. bonse banali bachilungamo kwa Mulungu, anali omvelela malamulo yonse ndimafano ya Mulungu. Koma banalibe mwana, chifukwa Elizabeta anali osabeleka, ndiponso bonse banali okalamba pali ijantawi. 8 9 10 Ndipo ntawi inafika pamena zachariya anali mumalo ya Mulungu, analikuchita nchito yake yaopeleka nsembe mundandanda yazigao.Kulinganiza nanjila yamwambo osankha wopeleka wansembe wamene angatumikile, analikusankha munjila yoteya njuga pongena mu tempele ya Mulungu kushoka nsembe.banthu bonse banali kupempelela panja panthawi ija yamene nsembe inalikushokewa. 11 12 13 Manje mungelo wa Mulungu anaonekela kwa iye ndikuimilila kumbali ya zanja lamanja yaguwa yansembe.Pamene Zachaliya anamuna, Iye anaopezedwa ndi Mantha. Koma mungelo ananena kwaiye, ''Usayope Zachaliya, chifukwa mapempelo yako zamveka.mukazi wako Elizabeta azakubalila mwana mwamuna.uzamuitana zinalache kuti Yohane. 14 15 Iwe uzankhala nachimwemwe ndi chisangalalo, ndiponso ambiri azasangalala kamba kakubadwa kwache. chifukwa azankhala wamukulu mu manso ya Mulungu. askamwepo vinyo olo zakumwa zobaba, ndiponso azazozedwa ndi muzimu oyela kuchokela mumimba yaba maibake. 16 17 Ndiponso banthu bambili baku isilaeli, bazapindimukila kwa Mulungu wao.Azaenda pamanso ya Mulungu mu muzimu ndi mphamvu za Eliya.Azachita izi pakupindimula mitima yabazitate kubanababo, kuti, ajaosamvelela baende munzelu zaolungama- ndikupanga banthu kukonzeka, ndikukonzekela Mulungu''. 18 19 20 Zakaliya ananena kwa mungelo, ''Kodi ninkazibe bwanji izi? chifukwa ndine okalamba ndi mukazi wanga naemve ni mukukulu.'' Mungelo anayankha ndikunena kwa iye, '' Ndine Gabuliyele,wamene amaimila pamanso ya Mulungu.Nenze natumiwa kulankula naiwe,kubwelesa uyu utenga wabwino.Ndiponso, uzankhala mwakacheta, ndikukangiwa kukamba, kufikila siku yamene izi zinthu zizafikiliziwa.Ichi nichifukwa chakuti, siuna kululupile mau yanga, yamene yazafikilisiwa pa nthawi yokwana.'' 21 22 23 Koma manje banthu banali kuembekeza Zakaliya, chenze kubadabwisa chifukwa chakuti enze kutayanthawi yambili mu tempele. koma pamene anachoka, sianali kukamba nabemve.Anazindikila kuti anaona mansompenya pamene anali mutempele. Anapitiliza kualangiza ziziwiso ndi kunkhala kachete.pamene nthawi ya masiku yake yotumikila yanasila, anayenda kunyumba kwake. 24 25 Panapita masiku ndi mukazi wake Elizabeta anamita.Anazipatulako eka mwezi isanu.ananena kuti, Azi ndiye zamene Mulungu anichitila pamene ananiyanganila na chisomo munjila yakuti anichoseko manyazi kubanthu. 26 27 28 29 Mumwezi wa chisanu nakamozi, mungelo Gabriel antumiwa ndi Mulungu kumuzinda oitaniwa nazaleti, kulinamwali wamene anali okobekelewa ku mwamuna wa zina la Yosefe. Analikuchokela munyumba ys Davidi, ndi zina yanamwali inali Mariya.Anabwela kwa iye ndikunene, '' Mulibwanji, inu odala! Ambuye alinanu.'' Koma anankala osokonezeka pamau yake ndikudabwa kuti kodi ungankhale moni wabwanji. 30 31 32 33 Mungelo ananena kwa iye, Usayope, Mariya, wapeza chisomo kwa Mulungu.ona iwe uzabeleka