Mutu 50

1 Ndipo Yosefe ana lemesedwa kwa kuti anagwa pa nkhope yake ba tate. Ndipo anamulilila eve, ndipo ana mu fyofyonta. 2 Yosefe ana lamilila a dotolo ba chito bake ku konza tupi ua tate bake. Sopano a dotlo ana konza Isreali. 3 Bana tenga masiku fote, pakuti inanli ntawi yakwanila kwakuti amukonze. Ba ku Egipito analila masiku okwanila seventi. 4 Pamene masiku olila ana sile, Yosefe anakamba ku nyumba ya Falao, anakamba, "ngati manje napeza mwai mu meso yako, napapata nikambileni kuli Falao kukamba kuti. 5 Ba tate banani Lepisa kukamba, "Ona nili pa fupi kufa. Ne shikeni mu manda mwamene niza zikumbila ine neka muziko ya Kenaani. Ukudiye muzanishika ine." Manje lekani ine niyende nika shike ba tate banga. Ndiponso nizabwelela. 6 Falao anayanka, "Enda ka shike ba tate bako ba, banani lapisa. 7 Yosefe ana yenda ku ka shika atate bake. Ba nchoti bonse ba Falao bana yenda na eve bakulu bakulu bonse muyumba yake. Bonse bamu ziko la Egipito, 8 na nyumba yonse ya yosefe ndi abale bake bonse, ndipo ba munyumba yabatate bake. Koma bana babo, Vobeta kabo, ndi ngobe zao zina sala mu malo ya Gosheni. 9 Golo ndi aka valo zina yenda beve cinali cigulu cacikulu cabanthu. 10 Pamene bana bwela ku malo yopepeptela ya Atadi kumbali ina ya Yolodani, ana lilila kwakululu movesa chifundo. Uku Yosefe ana panga ma siku asanu ndi ziwili kulila ba tate bake. 11 Ndipo onkhala mu ziko amu Kenaani, anaona kulila pasi ya Atadi, bana kamba, "Ici ni cisoni cacikulu kwa banthu ba ku Egipito." Chifukwa cake malo a itaniwa Abeli Mizraimu kupitilila Yodani. 12 Sopano bana bake ba Yakobo ana chita zamine ana ba lamulila beve. 13 Bana bake bamuna anamunyamula eve ku malo ya Kenaani ndi kumshika muci kwema mumunda wa machipela pafupi na Mamri . Abrahamu ana gula mukwema ndi munda malo yo shikilako. Anagula kwa Efuraimu ma Hititaiti. 14 Pambuyo yo shika ba tate bake. Yosefe ana bwelelela ku Egipito. Eve, pamozi na abale bake ndipo bonse ana mupelekeza eve mu shika ba tate bake. 15 Ndipo abale ba Yosefe pamene bana one kuti ba tate babo bafa, bana kamba manja ngati Yosefe akati nkalila naukali ise ndipo nakufuna kytibweza ise zoipa zose tina chita kwa eve? 16 Sopano bana lamulila ku pezekapo kwa Yosefe. kukamba kuti, "Ba tate banapasa malamulo bakelebe kufa kukamba, 17 Uzeni yosefe izi," napapa ba kukukila abale bako machimmoyabo ndi zolakwa zawo pamene bana chita zoipa kuli iwe." Manje napapata ba kukukile ba tumiki ba Mulungu ba batate bako." Yosefe analila pamene bana kamba na beve. 18 Ba bale bake futi ana yenda ndi kugona choyangana pasi pamaso pake. Bana kamba, "One, ndise ba nchito bako." 19 Koma Yosefe ana bayanka beve, "Musayope. kodi nilimumalo ya Mulungu? 20 Kwa iwe, munanifunila zoipa ine. Koma ana ni funila zabwino. Ku pulumusa miyo zaanthu ambili. Monga muona lelo. 21 Manje musayope nizakupasane vintu iwe na bana bangona anabalikisa beve munila yambwinno akukamba zabwino ku mitima yabo. 22 Yosefe ana nkhala mu Egiito, pamozi na banja yaba tate bake. Ana nkhala zaka 110. 23 Yosefe ana ona bana ba Ephraimu na bana bana badwa mumubada wachitatu, ndiposo ana ona bana ba Makira aba ba Muna ba Manase, ba mane ba Fakiwa pama nkhonkhola ya Yosefe. 24 Yosefe ana kamba kwa abale bake, "Nalipa fupi kufa, koma Mulungu zoona azabwela kwa imwe na kuku sogolelani kuku chosa mu malo yamene ana lapa ku pasa Abramu kwa Isaki ndi Yakobo. 25 Ndipo Yosefe ana panga bana ba muna ba Israeli kulapila pangano, "Mulungu chazoona aza bwela kwa inu. Patiwe ija mufunika muka yamule ma boza yanga kuyta chosa muno." 26 Sopano Yosefe anafa, na zaka 110 bana koza tupi yake ndi po ana ika mu bokosi ku Egipito.