mutu 35

1 Mulungu ana uza Yakobo, "nyamuka, yenda mpaka kufikila ku Bethe, Ndipo ankale kwamene kuja. Manga guwa kwamene kusa ya mulungu, wamene ana oneka kuli iwe pamene anataba kuli Esau mubali wako. 2 Ndipo Yakobo anauza ba munyumba yake na bonse bamene anali nabo, "ikani kutali tu milungu twa kunja twamene tuli naimwe, ziyeleseni mweka, ndipo chinjani vovala vanu. 3 Ndipo tiyeni tiyambeko na kuyenda mpaka kufikila ku Bethel niza manga guwa kuja ya Mulungu, wamene ananiyanka mu musiku yo tangwanika, na ku nkala naine kuli konse kwamene nayenda." 4 Mwaicho banamupasa Yakobo tonse mulungu twa boza twamene tunali mu manja mwao, na masikiyo ya mene yanali ku matu yao. Yakobo anayafwikila mangansi mwa mutengo wathundu unali pafupi na she chem. 5 Pamene banali kuyanda, Mulungu anapanga manta kugwela pa mizi zamene zanali kuba Sibaha bakonke bana ba Yakobo. 6 Mwaicho Yakobo anafaka ku Luz (amene inali Bethel), yamene inali kumalo yaku Kanaani, eye na bonse bantu bamene banali naye. 7 Anamanga guwa kuja na kupasa Mulungu anazi onesa kuli eve pamene anali kutaba ku chokela kuli mu bale wake. 8 Deborah, wachinto wa Rabekal, anafa. Anashikiiwa ku Bethel pansi pa mutengo wathundu, mwaicho bana itana malo yaja Allon Bakuthi. 9 Pamene Yakobo anabwela kuchoka ku Paddan Aran, Mulungu anaonekela kuli eve naku mudalisa. 10 Mulungu anakamba kuli eve, "Zina yako si Iza itaniwa Yakobo. zina yako izanikala Iseali." waicho Mulungu anamuitana zina yake Isreali. 11 Mulungu anakamba kuli eve, "ndiwe Mulungu wampamvu zonse. Kaba laneni na kupaka. Ziko na magulu ya maiko yazachoka kuli imwe, pa bana banu. 12 Malo yamene nina pasa iwe ku bana bo badwa mumbuyo mwako. niza bapasa malo." 13 Mulungu anachokako ku malo kwamene nanakamba na naye. 14 Yakobo anaika mwala ukulu pamalo pamene Mulungu anali ku kamba naye. Pila ya mwala. Anafilapo chakumwa kunkala ngati nsembe na mafuta. 15 Yakobo anaitana malo yamene Mulungu analikukamba naye, bethel. 16 Banali pa ulendo kuchokela ku Bethel, Rakel vumo inauka. 17 Pamene vumo inauka mo vuta, omubalisa anamu uva, "osayopa, apa manja uzankala na mwana mwamuna winangu. 18 Pamene anali kufa, anaku pema ko silizila anapasa zina mwana wake Ben-oni, koma atate bake banamuitana Benjamin. 19 Rakel anafa ndipo banamu shika munjila yo yenda ku efrata (ndiye Bethlehem). 20 Yakobo anaikapo mwala pa manda pake ni chozibilako pa manda pa Rakel mpaka lelo. 21 Isreali anayenda na kufika hema yake pasogolo pa yanganila vibeto vake. 22 Akali kunkala kumalo kuja, Reubeni anagona na Bilhah nukazi wa atate bake waku mbali, na Isreali ananvela pali iyi nkani. 23 manji Yakobo anali na bana bamuna 12. Bana bake kuli Leya banali Reubeni, mwana wkae oyamba, ana Simeoni, Levi, Yudah, Isacha, na Zebulani. 24 Bana bake kuli Rakel banali Yosefe na Banjamin. 25 Bana bake kuli Bilhah wa nchito wachikazi banali Dani na Naphatali. 26 Bana ba Zelipa, wachoto wa Leya mukazi, banali Gad, na Asher. Bonse aba banali bana ba Yakobo bamene anabala ku Paddan Aram. 27 Yakobo anayenda kuli Isaki atate bake, ku Mamre mu Kinah Arba ( chimozimozi Hebron) kwamene Abrahamu na Isaki banali ku nkala. 28 Isaki anankala zaka 108. 29 Isaki abapema ka kosilizila nakufa, ndipo anatengewa ku makolo yake, nkalamba ya masiku yambili. Esau na Yakobo, mwana wake mwamuna, banamushika.