Mutu 24

1 Bafuti kukalioa kwa Mulungu kunabwela pali ma Isilayeli, ndipo kamba kuti, "Yenda, penda Isilayeli na Juda." 2 Mfumu inakamba kuli Yowabu Mukulu waba nkondo wamene anali naye, "Yenda konse kumitundu ya Isialyel kufikila ku Beridhiba, naku penda bantu bonse, kuti nizibe baizmuna bonse pamoi bamene banga kwanise nkondo." 3 Yowabu anakamba kuli mfumu kuti, "Yehova Mulungu wanu Apakise bantu kali 100, na menso ya bwana wanga mfumu achione nichani bwana wanga mfumu afuna ichi?" 4 Koma, mau ya mfumu yenzeli yosilizila pali Yowabu na pali bazukulu ba nkondo. pamene apo Yowabu naba zukulu bankondo bana yenda kuchoka pamenso ya mfumu kupenda bantu ba Isilayeli. 5 Bana oloka Jodani naku nkala mufupi mwa Aroeri, mumuzinda wamu chigwa chaku mazulo kuchoka apo bamapitiliza kuyenda mu Gadi kufika ku Jaza. 6 Bana bwela ku Giliyadi baku ziko ya Tatimu Hodshiri, ku chokela apo kupitiliza kuyenda ku Dani Jani namu mbali kusogolo kwa Sidoni. 7 Banafika ku stronghold ya Tira, nayama Kenaniti. Chokonkapo bana yenda ku Negevu mu Yuda ku Beershiba. 8 Pamene bana yenda mu ziko yonse, bana bwelela mu Yelusalemu pakusila kwa myenzi ili nini nama siku yali 20. 9 Kuchoka apo Yowabu anabauza chibwelengelo chabonse bazimuna bandeo amfumu. Mu Isilayeli mwenzeli bali 800, 000 bolimbika dodansa lupanga, naba zimuna baku Yuda benzeli 500,000 baizmuna. 10 Chokonkapo mutima wa Davide unamuvuta pambuyo pobelenga baizmuna. Pamene apo anakamba kul Yehova kuti, "Nachimwa maningi pochita ichi. Manje, Yehova, tengani chimo manje yawa nchtio wanu, popeza nasobela mopusa maningi." 11 Pamene Davide anauka kuseni, Mau ya Yehova yanabwela kuli muneneli Gadi, mulauli wa Davide, kukamba kuti, 12 "Yenda ukakambe kuli Davide: 'Ichi ndiye chamene Yehova akamba: "Nikupasa chonsaka pali vitatu. Sankapo chimozi pali ive.""' 13 Pamene apo Gadi anayenda kuli Davide nakukamba kuli enve kuti, "Pa zaka zitatu ko yanu ku kubwelelani muziko yanu? Kapena kutaba pamene adani bako baku pilikisha kwa myenzi itatu? olo kapena kukankale matenda pama siku yatatu? Manje ganiza yanko yamene niza bwelzela iye wamene anituma ine." 14 Kuchoka apo Davide anakamba kuli Gadi kuti, "Nili muvuto ikulu. Lekani tigwela mumanja ya Mulungu kuchila kuti tigwele mumanja ya mwamuna, popeza kuchita kwa chifundo chake nikwa kulu maningi." 15 Pamene apo Yehova anatumiza matenda pali Isilayeli kuchokela kuseni kufikila pantawi yokwanisika, bantu bokwanila 70,000 banafa kuchokela ku Dani kufikila ku Beershiba. 16 Pamene mungelo anafikisa kwanja yake pasogolo kuti aononge Yelusalemu, Yehova anachinja nzelu chifukwa cha kuononga kwamene chiza chia, ndipo anakamba ku mungeli wamene enzeli ku wononga bantu, "Kwasila! Manje bweza kwanja yako." pantawi imilile potwel pa Arauna mu Jebusiti. 17 Chokonkapo Davide anakamba na Yehova pamene anaona mungelo wamene anabwela anaponya matenda pa bantu, naku kamba kuti, "Nachimwa, 'Naku sobela mu mpulumpulu. Koma nkosa iyi, Nivi chani vamene zachita? Napapata lekani kwanja yanu ini lange ine na banga yaba tate banga!" 18 Kuchoka apo gadi anabwela siku ija kuli Davide nakukamba kuli enve kuti, "Yenda pa mwamba naku manga guwa ya Yehova potwela pa Arauna mu Jebusiti." 19 Pamene apo Davide anayende pamwamba monga Gadi anmu langiza kuti achitte iye, monga Yehova analamulila. 20 Arauna anayanga panja naku ona mfumu naba nchito bake babwela. Pamene apo Arauna wayenda panja nakuzi chepesa kuli mfumu na nkope yake pansi. 21 Chokonkapo Arauna anakamba kuti, "Nichani bwanawanga mfumu abwelele kuli ine, wanchito wake?" Davide anayanka, "Kugula potwela, kuti nimange guwa ya Yehova, kuti matenda yachoke pa bantu," 22 Arauna anakmba kuli Davide kuti, "utenge ngati yanu, bwana wanga mfumu. CHitani nayo chamene chili chabwino mumenso yanu. Onani, aya ma oxani ya nsembe yoshoka navotwela nama goli ya nkuni. 23 Vonse ivi, mfumu yanga, Ine, Arauana, nizaku pasani." kuchoka apo anakamba kuli mfumu kuti, "Yehova Mulungu wanu akuvomeleni imwe?" 24 Mfumu anakamba kuli Arauna kuti, "Iyayi, nizaigula pamutengo siniza peleka ngati sembe yoshoka kuli Yehova chilichonse chamene sichinalipiliwe kali konse. Pamene apo Davide anagula potwela nama oxeni kwama shekeli yasiliva yalififite. 25 Davide anamanga guwa ya Yehova kuja naku peleka nsembe yoshoka na nsembe yanu sonkano. Pamene apo Yehova anayanka pempelo pamalo pa ziko, na matenda pali Isilayeli yana lekeza.