Mutu 22

1 Davide anaimbila Yehova mau yanyimbo iyi pasiku yamene Yehova anamupulumusa iye kuchokela mumanja mwa ba dani bake, namu ma ja mwa Saulo. 2 Anapempela, Yehova ni mwala wanga, tantwa langa, mupulumusi, wamene amani pulumusa ine. 3 Mulungu ndiye tanwe langa. Iye ndiye kotabila kwanga. Ndiye chikopa changa, nyanga ya chipulumuso changa, chitetezeo changa, nako tabila kwanga, iye wamene anandi amanichosa kuchokela ki nkanza. 4 Niza itana pali Yehova, wamene ayenela kumu tamanda, ndipo nipulumusiwa kuchoka kuli ba dani banga. 5 Pakuti mafunde ya imfa yanani zunguika ine, manzi yo tamanga ya chiongeke yanazininga ine. 6 Chingwe chaku Sheolo yananizi nguluka ine. Misampa ya infa inani valiza ine. 7 Muchisoni changa nina itana kuli Yehova; Nina itana kuli Mulungu wanga ananvele mau yanga kuchokela mutempele yake, naku itana kwangkuti anitandize kunyanda mumatu mwake. 8 Kuchoka apo ziko ina nyanganya naku njenjema. Maziko yaku mwamba yana njenjema ndipo yana nyanga nyisiwa, chifukwa Mulungu enzeli okalipa. 9 Chusi chinayenda mumwamba ku chokela mupuno mwake. Malasha yana yashiwa nayo. 10 Anasegu mumwamba nakubwela pansi, mpizi ikulu inali pansi pa mendo yake. 11 Anakwela pa kerubi naku mbululuka. Anaonewa pama piko yachimpepo. 12 Anapanga mfizi ngati hema mumbali mwake. Kufaka pamozi makumbi ya nvula ikulu mu mwamba. 13 Kuchokela kukaleza pamenso pake malasha yamulilo yanagwa. 14 Yehova anagunda kuchokela kumwamba. Wakumwamba mukulu anapunda. 15 Anautumiza mivi naku mwaza adani bake-kuyasha mpezi naku bamwaza iwo. 16 Kuchoka apo ngalande zamu nyanja zinaoneka; maziko ya muziko yosavala yanailaka pakuzuzula kwa Yehova paku chinga kwa kupema kwa mpuno zake. 17 Afaika pansi kuchokela kumwamba anamu gwila iye! ananichosa ine kuchokela mu manzi yalina mpavu. 18 Anani pulumusa ine kuchokela kuba dani banga ba mpavu, kuchokela kuli abo benze ba mpavu kuli ine. 19 Bana bwela pali ine pasiku ya chisoni changa, koma Yehoba enzeli wonitandiza. 20 Ananileta futi panja pamalo yoseguka maningi Ananipulumusa chifukwa enzeli wokondwela naine. 21 Yehova anipasa malipilo kulingana na chilungamo changa, Anibwezela ine kulingana naku yela kwa manja yanga. 22 Pakuti na sunga njila za Yehova, ndipo sinina chite voipa monga kusiya Mulungu. 23 Pakuti kuweluza kwake kwa chilungamo kwenzeli pa menso panga, koma malemba ake, sininayachokemo. 24 Ninali futi osalakwa pamenso pake, naku zisunga kuchoka ku chimo. 25 Chaicho Yehova anibwezela ine kulinga namuyeso wachilungamo changa, ku malamulo yakuyela kwanga mumenso mwake. 26 Kuli okulupilika mumazilangiza okukulupilika kwanu; kuli mwamuna wamene alibe choipa chili chonse, mumazi langiza osaipa chili chonse kwanu. 27 kuli boyela mumazi langiza kuyrla kwanu, koma ndimwe boipa kuli ab boipa. 28 Muma pulumusa bantu bonzunzika, koma menso yanu siyafuna bozikweza, ndipo mumaba bweza pansi. 29 Popeza ndimwe nyali yanga, Yehova. Yehova amayasha mudima wanga. 30 Popeza pali imwe ninga tamange pali kuchinga apli Mulungu wanga ninga jumpe pamwamba pa chipupa. Koma Mulungu, njila zake nizangwilo. 31 Mau ya Yehova niyo yela. Ndiye chikopa cha aliyense wamene atenga kuchingiliziwa muli enve 32 Popeza nindani Mulungu kunja kwa Yehova, elo nindani mwala ukulu kumbuyo kwa Mulungu watu? 33 Mulungu ndiye chochingiliza changa, ndipo amayenda bantu balibe choipa chili chonse munjila yake. 34 Amapangisa mendo yanga yasanduka manga ya mbwalala naku mfaka pa mwamba pama pili. 35 Amapunzisa manja yanga kumenya nkondo, na tukumo twanga kubendeka uta wansimbi. 36 Munani pasa ine chozi chingilizila chakutumikila kwanu, kufafasa kwanu kwanipangisa kunkala mukulu maningi. 37 Mwapanga malo yoseguka kuti mendo yanga yasatelele. 38 Nina piliksha adani banga nakuba ononga. Sininabwelele paka naba ononga. 39 Ninabasiliza nakuba pwanya; Sibanga nyamuke, Bagwa kumendo yanga. 40 Mufaka mpavu pali ine manga lamba ya nkondo: Mufaka pansi panga aba bamene baninyamukila ine. 41 Munanipasa kumbuyo kwamukozi waba dani banga; Nina onogelatu baja bamene banali kunizonda. 42 Banalilila tandizo, koma kwenzelibe oba pulumusa. Banalila kuli Yehova, koma sanabayanke. 43 Nina bamenya mutu gawo tungono tuli monga doti ya pansi, munaba ononga monga matika yamunjila. 44 Munanichisa futi ine kuchokela muku yambana kwabantu banga mwani sunga ine ngati mukulu wama ziko. Bantu bamene sinenzo bana zipeleka kuli ine. 45 Baku ziko yachilendo benze kupati kiziwa kuzi chepesa kuli ine. Pamene chabe banvela zaine, banani mvelela ine. 46 Baku ziko yachilendo bana bwela na manta kuchokela kuzobagwilila. 47 Yehova niwamoyo! Mwala wanga ukulu utamandike. Mulungu akwezekedwe, mwala ukulu wa chipulumuso changa. 48 Uyu ndiye Mulungu wamene amaleta chilango chofukwa chaine, Iye wamene amaleta pasni bantu bamene bali pansi panga. 49 Amandi masulu ine kuchokela kuba dani banga. zo-ona, munaninyamula kunifaka pamwamba pa abo bamene banani nyamukila ine. Munadi pulumusa kuchokela kubazimuna bachi wembu. 50 Chaicho nizapeleka chiyamuko kuli imwe Yehova, pakati kama ziko; nizaimba matamando kuli zina yanu. 51 Mulungu apasa kupambana kukukulu kuli mfumu yake, naku langiza chipangano chokululupilika kuli azozewa wake, kuli Davide naku mibadwo yake muyayaya.