Mutu 15

1 Chinafika kuti patapita ivi pamene Abisalomu anakonzekela gareta na akavalo ba enve eka, naba muna bali fifite botamanga kusogolo kwake. 2 Abisalomu enzeli ku ukakuseni naku imilila pambali yanji;a yoyenda ko ngennela kwa muzinda. Ngati mwamuna aliyense aliyense alina nkani ku bwela kuli mfumu kuti aweruze. 3 Ndipo Abisalomu enzeli kukamba kuli iye kuti, "Ona, nkani yako niyabwino nayo lungama, koma kulibe opasiwa mpavu naba mfumu kunvela nkani." 4 Abisalomu anapitiliza, "Asembe ninali namulilo mu ziko, kuti aliyense mwamuna wamene ali na mulandu wake kapena chifukwa chake abwele kuli ine, ndipo nizamupasa zachilungamo. 5 Chinachitika kuti ngati pamene aliyense mwamuna abwela kuli Abisalomu kumu lemekeza Abisalomu anali kuchosa kwanja nakumu kumbata iye naku mu myompyota. 6 Abisalomu anachita ivi kuma Isilayeli bonse bamene banali kubwela kuweluziwa kuli mfumu. Abisalomu anagwila mitima zabazimua bamu Isilayeli. 7 Chinachitika kuti pakusila kwa zaka folo pamene Abisalomu anakamba kuli mfumu kuti, "Nipempa kuti niyenda naku lipila kulumbila kwamene nina panga kuli Yehova mu Hebroni. 8 Pakuti wanchito wanu analumbila pamene ninali kunkala ku Gesha Arami, kukamba kuti, 'Ngati zo-onadi Yehova azanibweza ine futi ku Yelusalemu chokonkapo nizamu tamanda Yehova.'" 9 Pamene apo mfumu anakamba kuti, "Yenda mu mutendele." Pamene apo Abisalomu ananyamuka naku yenda ku Hebroni. 10 Koma chokonkapo Abisalomu anatuma bozanda muli zonse mutundu za Isilayeli. Kukamaba kuti, " Pamene chabe muzanvela chongo chalipenga, chokonkapo mukazmbe kuti Abisalomu ndiye mfumu mu Hebroni.'" 11 Naya Abisalomu kumayenda bazimuna bali 200 bochokela mu Yelusalemu, bamene bana itaniwa. Bana yenda mosaziba, Mosaziba vili vonse vamene Abisalomu anakonza. 12 Pamene Abisalomu anali kupeleka nsembe, anaitana Ahitopelo kuchokela mumuzinda wake wa Gilo. Enzeli Mulangizi wa Davide. CHiwembu cha Abisalomu chinali cholimba, kukonka Abisalomu benzel ku pakilako. 13 Ntumwi anabwela kuli Davide kukamba kuti, "Mutima zaba zimuna mu Isilayeli za kanka pali Abisalomu." 14 Pamene apo Davide anakamba bamkuli bonse banchito bake bamene benzeli mu Yelusalemu naye kuti, "Nyamukani kulibe kapena umozi waise wamene azamutaba Abisalomu. Konzekani kuchoka manje, pakuti azati pitilila mwamusanga ise, ndipo azaleta ngozi pali ise nakuti menya mumuzinda na mpempeta ya lupanga." 15 Wanchito wa mfumu anakamba kuli mfumu, "Onani, banchito bako nibo konzeka kuchita vilivonse vamene mbuya wanga mfumu iza ganizaila." 16 Mfumu inayenda na banja yonse naye, koma mfumu anaiya bazikazi bali teni, bamene nalai bamai nini kuti basunge nyumba yachifumu. 17 Pamene mfumu anayenda nabantu bonse naye, banaimilila pa nyamba yosilizila. 18 Bankondo bake bonse banayenda naye, pali banayenda naye kunali ba Keretitisi, na bonse ba peletitisi, na bonse ba Gititisi-bazimuna bokwanila 600 bamene bana mukonka kuchokela ku Gati. 19 Chokonkapo mfumu inakamba kuli Ittai mu Gittiti, "Chifukwa nichani chamene uzatikonkela ise? Bwelela ukankale na mfumu, popeza ndiwe wachilendo nabo pita bwelela kumalo yako. 20 Popeza kuti unachokako zulo nichani chamene nizakupangisa kuti uzi yenda chiyende yende konse konse naise? Siniziba ukatenge abale bako, chikondi chilonkazikika na chikulupililo viyende naiwe." 21 Koma Ittai anayanka mfumu anku kamba kuti, "Malinga Yehova ali wamoyo, na bwana mfumu yanga ali na moyo, nditi kumalo yali yonse kwamene bwana wanga mfumu azayenda, uko naye wanchito wanu azayenda kapena chitantauza umoyo kapena kufa." 22 Davide anakamba kuli Itai, "Pitiliza kuyenda naise." Itai mu Gitite anapiliza kuyenda namfumu, pamozi nabazimuna bake na mabanja yake yonse yamene yanali naye. 23 Ziko yonse inai mokwezeka mau pamene bantu benzeli kupita pamwamba pa chigwa yake Kidroni, na pamene mfumu ine yake inawoloka. Bantu bonse banyenda njila yaku chipululu. 24 Na Zadoki nama Levitis bonse, monyamula likasa yachipangano cha Mulungu, banalipo. Bana faka likasa ya Mulungu pansi, chokonkapo Abiata anagwilisana bonse bapita kuchoka mumuzinda. 25 Mfumu anakamba na zadoki kuti, Nyamula likasa ya Mulungu kubwelela mumuzinda. Ngati nizapepa chisomo mu menso ya Yehova, Azani bweza kuno ine naku nilangiza futi likasa napa malo pamene ankala. 26 Koma ngati azakamba kuti, sindine wokondwela naiwe,' onani, ndine pano, leka kuti achita kuli ine chamene chioneka chabwino kuli enve." 27 mfumu inakamba futi kuli Zadoki wansembe kuti, "Nanga sindiwe miauli? Bwelela mumuzunda mwamu tendele nabana bako bamuna, Ahimaazi mwana wako mwamuna, na Jonatani mwana mwamuna wa Abiata. 28 Ona nizalindila kuma fordi ya Araba paka mau yaka choke kuli iwe kunizbisa ine." 29 Pamene apo Zadoki na Abiata bana nyamula likasa ya Mulungu kuibweza mu Yelusalemu ndipo banankala kwamene kuja. 30 Koma Davide anakwela kosoba nsapato kumendo naku lila pa mwamba pa mapili ya Olivi, ndipo anavininkila mutu wake aliyense mwamuna pali bantu bamene enze nabo anavinikila mutu wake, bana yenda pamwamba ndishi balila kwinangu bayenda. 31 Winangu anauza Davide kukamba kuti, "Ahitopelo niumozi waba chiwembu alina Abisalomu." Davide anapempela, "Inu Yehova, sandisani malangi ya Ahitpoelo kunkala upuba." 32 Chinafika kuti pamene Davide anafika pamwamba pa njila, pamene banaliku labila Mulungu Husai waku Arkiti anabwela ku kumana naye nachovala chake chongambika namutu wake pa ziko. 33 Davide anakamba kuli iye, ngati uzayenda naine, uzanivutisa ine. 34 Koma ngti uzabwelela ku muzinda naku kamba kuli Abisalomu kuti, 'Nizankala mwanchito wako, mfumu, monga mwamene nenzelili wanchito wa batate bako kudala, ndiye mwamene nizankalila wanchito wako, kuchoka apo uzasokoniza chilangizo xha Ahitopelo pamalo panga. 35 Nanga suzankala na wansembe Zadoki na biata na iwe? chilichinse chamene anzanvela munyumba ya mfumu, ufunika ukaziuza Zadoki na Abiata wansembe. 36 Ukaona kuti balinaba kuja bana babo bamuna, Ahimazi, mwana mwamuna wa Zadoki, na Jonatani, mwana mwamuna wa Abiata. Ukazituma vonse vamene wanvela mumanja mwao." 37 Pamene apo Hushai, muzake wa Davide, anabwela mumuzinda pamene Abisalomu anafika naku ngena mu Yelusalemu.