Mutu 13

1 Chinachitika kuti patapita izi pamene Amoni mwana mwamuna wa Davide enze ku kumbwila mulongo wake wamene sanabadwa naye wabwino wa ABisalomu wobadwa naye, winangu wabana bamuna ba Davide. 2 Amoni anankala onzunzika paka anadwala chifukwa chamulongo wake Tama. Enze akali namwali, ndiye chinankala chovuta kuti Amoni achite chilichonse kuli iye. 3 Koma Amoni enze anli namunzake wamene zina yake ni Jonadabu mwana mwamuna wa Shimiya, mubale wa Davide. 4 Jonadabu anali mwamuna wanzelu zoipa. Jonadabu anakamba kuli Amoni kuti, "Nichani, mwana mwamuna wa mfumu, umanka unzunzi kuseni kuli konse? Nanga siuzaniuza?" Amoni anamuyanka iye kuti, Nikonda Tama, mubale wanga mulongosi wa Abisalomu." 5 Kuchoka apo Jonadabi anakamba kuli enve kuti, "gona po gona pako naku zipanga kwati wadwala. Pamene batate bako bazabwela kukuona, ubapempe kuti, "Nanga munganitiuzileko Tama mulongo eanga kuti anileteleko chintu chamene ningadye naku chipika pa menso panga kuti nichione nakudyela mumanja yake?'" 6 PAmene apo Amoni ana gona nakuzipanga kudwala. Pamene ba mfumu bana bwela kumuona iye, Amoni anakamba kuli ba mfumu, "Napapata nitumileni mulongosi wanga Tama kuti anipangile vakudya pa vodwala vamga mumenso mwanga kuti nidye mu manja wake." 7 Pamene apo Davide anatuma mau kuli Tama kunyumba yake ya chifumu, kukamba kuti, "Yenda manje kunyumba ya Amoni mubale wako kuti ukamukonzele chakudya iye. 8 Pamene apo Tama anayenda kunyumba ya Amoni mubale wake kwamene enzeli gone pansi. Antenga vokandiwa va flaulo nakuvikonza naku panga mukate pamenso pake, nakupika. 9 Anatenga pani nakumupasila mukate iye, koma anakana kudya. chokonkapo Amoni anakamba nabantu benzemo kuti, "bachoseni bonse, muli ine. "Pamene apo bonse banachoka mwamene enzelili. 10 Amoni anakmba kuli Tama kuti, "Leta vakudya muchipinda changa kuti tidye kuchokela mumanja yako. "Ndipo Tama anapeleka mukate wamene anabwela apanga, naku uleta muchipinda mwamubale wake Amoni. 11 Pamene analeta chakudya kuli enve, anamugwila iye nakukamba kuli enve kuti, "bwela ugone naine, mulonga wanga." 12 Anamuyanka iye kuti, "Iyayi, mubale wanga, usanipatikize sichifunika kuchitika mu Isilayeli. Usachite ichi chintu chonyansa! 13 NInga chose bwanji nsoni zanga? nanga iwe? uzankala moga umozi wavipuba mu Isilayeli manje napapata kamba na mfumu, pakuti sibaza kusunga kuchaka kuli ine." 14 Koma Amoni sanamunvelele iye, futi enzeli nampvu kuchila enve, anamugonjesa iye, nak gona naye. 15 Pamene apo Amoni ana zanda Tama nachi zondo chambili. Ana muzonda maningi iye kuchila nachilako chamene enze nacho pali enve. Amoni anakamba kuli enve kuti, "Nyamuka naku yenda." 16 Koma anamuyanka iye,"kuti, iyayi chifukwa cholakwa chachikulu cholengesa kuti niyende nichikulu kuchili vamene wanichita iye. 17 Mumalo mwake, anaitana wanchito wake naku kamba kuti, muchose mukzai kuchoka kuli ine, nakuvalako kuchiseko akachoka iye." 18 Kuchoka apo banchito bake banamuleta panja naku koma chiseko ata choka iye. Tama enzeli anavala chovala chopangiwa bwino chifukwa bana bakzi banfumu bana mwal benzeli ku vala sochabe. 19 Tama anafaka pulusa pa mutu pake naku ngamba chovala chake. Anafaka manja yake pa mutu naku chokako, ku mo kuwa pamene enzeli kuyenda. 20 Abisalomu mubae wake anakamba kuli enve kuti, "Nanga Amoni mubale wako anali naiwe? Koma manje puzya, mulongo wanga Nimubale wako. Usachifakilile kumutima ichi." Ndipo Tama ansala eka munyumba yamu bale wake Abisalomu. 21 Koma pamene mfumu Davide anavinvela vonse ivi, anakalipa maningi. 22 Abisalomu sanakambe vili vonse kuli Amoni, pakuti Abisalomu enzeli kumuzonda chifukwa chavamene anabwela achita kuli iye namwamene anasebanyila Tama mulongo wake. 23 Chinafika kuti panapita zaka zokwanila zibili pamene Abisalomu anankala nabo bosebesenza kudyesela mbelele ku Baal Hazo, yamene ili pafupi na Eframu, Abisalomu anabaitana bonse bana bamuna ba mfumu kuti bamu tandalile kuja iye. 24 Abisalomu anayenda kuli mfumu naku kamba, "Onani manje, wanchito wanu alina bodyesela mbelele. Napapata, kuti mfumu na banchito bake bayende naine, wanchito wanu." 25 Ba mfumu bana muyanka Abisalomu, "Iyayi mwana wanga wamuna, Tizayenda tonse chifukwa tingankale vuto kuli iwe. "Abisalomu anapapata kuli mfumu, koma sana kwanise kuyenda, koma anamupasa madiliso yake. 26 Chokonkapo Abisalomu anakamba kuti, "Ngati siso, nipempa kuti mubale eanga Amoni ayende naise." Apa ba mfumu banakamba kuli iye, "Nichifukwa chani chamene Amoni azayendaele naiwe?" 27 Abisalomu anapitikiza Davide, ndiye anamuleka Amoni kuti nabonse bana bamuna bamfumu kuti bayenda naye. 28 Abisalom analamulila banchtio bake kukamba kuti, "Mvelani pafupi, pamene Abisalomu aza yamba kusokonezeka na vinyula napamene nizakamba kuli imwe kuti, kogesani Amoni, 'chokonkapo mumupaye iye. musankale boyopa. Nanga sina kulamulileni? Nkalani bolimba naku chenjela." 29 Apa banchito ba Abisalomu banachita monga mwamene Abisalomu anaba lamulila kuti bachite. Kuchoka apo bonse bana bamuna ba mfumu bana nyamuka, ndipo mwamuna aliyense anyamuka nakukwela bulu yake baku taba. 30 Chinachitika kuti, pamene benzeli bakali pa njila, pamene utenga unafika kuli Davide kukamba kuti, "Abisalomu apaya bana bamuna ba mfumu bonse, ndipo kulibe olo umozi asalako pali benve." 31 Chokonkapo mfmu inaimilila naku ngamba vovala vake, naku gona pansi; Bonse banchito banaimilili pali iye navovala vongambika. 32 ` Jonadabu mwana mwamuna wa Shima, mubale wa Davide, anayanka naku kamba kuti, "Lekani mbuya wanga asakulupilile kuti bana bafana bamuna banfumu bapaiwa, popeza kuti Amoni chabe eka ndiye Afa. Abisalomu anavi konza ivi kuchokela pasiku yamene Amoni anachita voipa kuli Tama mulongo wake. 33 Chaicho ichi chisalenge kuti mbuye wanga afakile ichi ku mutima, ngankale kukulupila bafa bamua bonse banfumu bafa, popeza Amoni eka ndiye afa." 34 Abisalomu anatba. Wanchito woyanganila ananyamula menso yake ndipo anaona bantu bambili babwela panja yalupili ya kumazulo kwamene enzelili. 35 Kuchoka apo Jonadabu anakamba kwa mfumu kuti, "Onani, Bana bamfumu bamuna ba bwela. Chili mongs mwamene wanchito wanu akambila." 36 Chinachitika kuti pamene anasiliza kukamb, bana bamfumu bamuna banafika naku lila mokwana. Mfumu nabonse banchito bake banalila kwakulu. 37 Koma Abisalomu anataba naku yendsa kuli Talmai mwana mwamuna wa Ammihud, mfumu ya Gesha. Davide enzekulila mwana wake mwamuna masiku yonse. 38 Pamene apo Abislomu anatba nakuyenda ku Gesha. kwamene anankala kwa zaka zitatu. 39 Nzelu zanfumu Davide zinafunisisa kuyenda kumuona Abisalomu, popeza anatontola paza Amoni na infa yake.