Mutu 16

1 A farisi ndi a Saduki anabwela kumuyesa naku pempa kuti alangize chizindikilo kuchoka ku mwamba. 2 Elo anayankha nakuti kwa iwo,''Ngati ni kumazulo, mumakamba kuti, 'kuzankala mpepo yabwino, ndaba ku mwamba kwaoneka ku sweta.' 3 elo kuseni muma kamba kuti, 'izaipa mpepo lelo, ndaba kumwamba kwa sweta elo makumbi yavininkila m'malo yonse, ' Muziwa kulondolola maonekedwe ya m'mwamba, koma simukwanisa kulondolola zizindikilo za ntawi. 4 mubadwe Oipa ndi wa chigololo umasakila zizindikilo, koma kulibe zizindikilo ziza pasiwa koma zizindikilo za Yonah,'' Pamene apo Yesu anawasiya nakuchokapo. 5 Pamene opunzila anafika ku malo yena, anabwe aibala kutenga mukate. 6 Yesu anati kwa iwo, ''onesesani ndiku chenjela na cho fufumisa cha a Farisi ndi a saduki.'' 7 opunzila anakambisana beka beka na kuti, '' Nichifukwa chakuti sitina tenge mukate.'' 8 Yesu anali kuziwa pali izi na kuti, ''Imwe a chikulupirilo ching'ono, nichani mukambisana pali imwe mweka nakuti nichifukwa chakuti simunatenge mukate? 9 Nanga simuganizila na manje naku kumbukila mikate ili five kuli ali five thousandi, nama basiketi niyangati yamene muna doba naku ika pamozi? 10 Nangu mikate seveni kuli four thousandi, nama basiketi yamene muna doba? 11 Ni bwanji kuti simu ziwa kuti sinenzeli kukamba kwa imwe pali mkate?Nkalani olanganisisa ndiku chenjela kwambili na chofufumisa cha a farisi ndi a saduki.'' 12 manje banaziwa kuti sanali ku kamba kuti ankale ochenjela na chofufumisa cha mu mkate, koma kuti ankale ochenjela nama punziso ama Farisi ndi a Seduki. 13 Manje pamene Yesu anabwela ku malo kufupi na Caesarea Filippi, anafunsa opunzila ake, ati, '' anthu akamba kuti Mwana wa Munthu ni ndani?'' 14 bana kamba kuti, ''ena amati Yohane Mubatisi; ena, Eliyah; na ena, Yeremiah, nangu umozi pali a neneli.'' 15 Anakamba kwa iwo, nanga imwe mukamba kuti ndine ndani?'' 16 Kuyanka, Saimon Petro, Anakamba kuti, ''Ndimwe Kristu, Mwana wa Mulungu wa moyo.'' 17 Yesu anayanka naku kamba kwa iye, ''Ndiwe odalisika, Saimon Bar Yonah, ndaba tupi ndi gadzi sivina ziwitse izi zinthu kuli iwe, koma Atate anga Ali kumwamba. 18 Ine anso na kamba kwa iwe kuti ndiwe Petro, ndiponso pali uyu mwala niza manga m'pingo wanga. Wamene ziseko za gehena siziza kwanisa ku gonjesa 19 Nizakupasa ma kiyi ya ku Umfumu wa Kumwamba. Zili zonse zamene uzamanga pa ziko naku mwamba ziza mangiwa, ndiponso zamene uzamasula pa ziko ziza masuliwa naku mwamba. '' 20 apo Yesu anakamba kuli opunzila ake kuti asauze muntu ali ense kuti ni Kristu. 21 Kuyambira pali iyo ntawi Yesu anayamba kuwa uza opunzila ake kuti afunika ku enda ku Yerusalemu, kuka vutisidwa kwambili mumanja mwa akulu a antu, akulu a nsembe ndi alembeli, ku paidwa, ndiku usidwa futi ku umoyo pa siku la chitatu. 22 Elo Petro anamutenga pambali nakumu kalipila, kuti, ''Lekani izi zinkale kutali naimwe, Ambuye; izi zisachitike kwa imwe.'' 23 Koma yesu anapindamuka nakukamba kwa petro, ''enda kumbuyo kwanga, Satana! Ndiwe chokumudwisa kwa ine, ndaba siusamalila pali zintu za Mulungu, koma zintu za antu.'' 24 Koma yesu anakamba kuli bopunzila bake, ''ngati aliyense afuna kunikonka ine, afunika azikane eka, kutenga M'tanda wake, nakunikonka ine. 25 Ndaba aliyense wamene afuna ku pulumusa umoyo wake azau sowesa, elo aliyense wamene asowesa moyo wake kamba ka ine azaupeza. 26 Nanga ni pindu ya bwanji ngati munthu akala nalo ziko lonse nakutaya umoyo wake? Nichani chamene munthu anga pase kuchinjanisa na umoyo wake? 27 mwana wa munthu azakabwela mu ulemelelo wa Atate ake ndi angelo ake. ndiponso azalipila muntu aliyense kulingana na zamene ana chita. 28 ndiku uzani, palili benangu pali imwe bamene bali imilile pano, bamene sibaza laba infa mpaka bakaone mwana wa munthu kubwela mu Umfumu wake.''